Email a copy of 'Supreme Court of Malawi dismisses State appeal on UTM registration' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Supreme Court of Malawi dismisses State appeal on UTM registration' to a friend
Malawi Law Society and governance expert have said President Peter Mutharika’s decision to remove Vice-President Saulos Chilima on protocol list...
What if one goes to register united transformation movement without abbreviations? Will utm complain?
UTM ndi ANGUNGA
DpP intha ngati moto wama pesi ukalimbana ndi Chilima…
Amfumu, this, like the staged theft of the biometric voter registration kit, has everything to do with DPP because there are no longer independent thinkers in government and parastatal organizations. Every leading officer there is a puppet controlled by State House or Ben Phiri.
Kikikikiki koma a pumbwa awa azunguzidwa mitu, zowona thuka phuu kulimbana ndi UTM. Koma utm ya patali na
so who will be fired today???…. kikikikikikikii
Wow koma izi wina alowa Mmanda mofulumira sure, ma British petrolium okhaokha makomomu, chonde mudzikhala nawo pafupi angagwe inu palibe. oyenda ndi lupanga ndi lupanga lomwelo adzafa nalo, muyeso omwe umamuyesa nawo nzako omwewo umaza kwa iwe mwini. UNE KUPOCHERA KWABASI
What has this to do with DPP? Is the DPP Registrar of political parties? I’m 100% behind DPP and will vote for APM! Problem with people is: when supporting their side they think the other side is a bunch of fools. Come 2019 UTM won’t get even a million votes! Mark my words. Only MCP can put up some challenge to DPP. Utm will drown into political oblivion come May 21, 2019. Pitilizani kulubwalubwa.
Pitiliza kulota aise maloto samaletsa koma wanzeru akudziwa komwe bomali likupita. Its clear kuti apumbwa sangawine or patavuta bwanji…plot yao iliyonse ikubwera pambalambanda. Zawavotere aise ife takwera yowina. Kkkkkkkkk moto buuu
DPP bunch of fools
If wishes were horses beggars would also ride.
Komatu kuayluka kulipo ndipo sanati … muoe ikatha parilament muva akuti apita uku ..iyi ikhala time yowawitsa kwa pumbwa moti adzikomzekera ma BP enieni osati iziz
Kodi nkhani ya a chikulire kufuna kunyenga supreme court judges kuti UTM isalembedwe ndiyowona? MK200 Million???????? Madzi achita katondo ngati ndizowona
DPP tingoyigulira chitenje choti wina alira