Email a copy of 'Swaziland club interested in Bullets defender Fodya' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Swaziland club interested in Bullets defender Fodya' to a friend
Malawi’s reggae power house the Black Missionaries popularly known as ‘Ma Black’ are ready to invade the capital city Lilongwe...
Yamikani wishing you all the best, pankhani ya tsisi wina asakuuze chochita m’bale wanga awa nde a Malawi amafuna paliponse apeze chonena(aliyense ali ndi style yake ngati enanu sizikusangalatsani akamasewera musamaonerere mpira till muzapeze oti azizatsatira zofuna zanu). May the good Lord continue blessing you Yamikani. God bless BB.
Big up to yamikani fodya when you travelling to swazland.God bless u
Akamete mohoko kunjako uyudi wanyanya, ngati nsing’anga???
Yamikani mulungu mudzina lako
Amenewo ndiye maule, fodya mo fire
I’m wishing you all the best Yamikani Fodya God bless you my dear,we (Mapalestina) will miss you so much bcz umatimvetsa kukoma mwana iwe wamkaka always,ukapitilize zi ntchito zako zabwino ku Swaziland,umakwana mfana BIG UP!!!!!!!!!!!!!!
Fodya sayamika.
Chitimutu ichooooooooo!!!!!! Wch mins timuyi ikusewera bwino umboni wake ndiwumenewu.
I strongly believe that we should first of all finish the league before we start selling players.
ZAZIIIII KU SWAZILAND? TAMETANI DZIMATSITSIZO! AFRO DZACHIKALE.