Email a copy of 'Tay Grin prepares for DPP primaries, rolls out campaign to contest as MP' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

34 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Hatton
Hatton
5 years ago

Kongilesi ndiye ai. Mavoto onse Ali mdelali ndizosamveka kuti kunali chipani chomwe chinalamula dzikoli zaka 31. Zoona a kongilesi mungasiye delali maliseche chonchi. Chomwe mumadziwa kunali kubwera mdelali kudzatolera ndalama za makhadi Kwa amai oyembekezera powagulitsa khadi la mwana woti sanabadwe. Voti yanga pamodzi ndi mavoti a anthu onse okonda Malawi ndi ya Kalilani. Kongilesi ndi nyansi.

Kaitano
Kaitano
5 years ago
Reply to  Hatton

Ubwino wake election ndi next yr,so take your heart and chill.
The Egyptians you see them today,you will not see them again.
Zimunamizani polongosola mmene Congress inalili, koma Ife tikuti it was a brilliant idea kukhala ndi Card, that is why today mukupatsa ma ID kwa obwera chifukwa chaumbuli.

Grace
Grace
5 years ago
Reply to  Hatton

MCP does not need your vote, you have never been MCP so don’t waste your time.

Ndalema
Ndalema
5 years ago

Tired of Banda’s, Mutharika’s, muluzi s, chakwambas, Tembos, Kadzamiras, Ntabas, Mpinganjiras, Dausis, Kaliranis, nankhumwa s, Mullis, mwanamvekas , Chapondas ndi zina zotero

mediaz
mediaz
5 years ago

Ma plan akuthera eti?Akunamiza ndi amako zimenezi?Iweyo ndi makoyo simuzawina,,,,,kkkkk….MCP bomaaaaaa!!!!!!

mtete
mtete
5 years ago

Tay Green? Ndiye kuti chiani?

Mchewa
5 years ago

Seriously the dreadlocks are distorting your figure people won’t vote for you because of your negative impression

Ntumbuka Weni Weni-Wapachitimba

Me I will vote for Alfred Jiya of MCP, this young man started development work long time ago osati moto wamapesi wabwerawu.Taygreen he eats take away from citymall ( Saphika odala) nde sangatithandize saziwa mavuto a mugetto

Maliseche
Maliseche
5 years ago

Malawians are sick and tired of the same old names in politics!!!!…….it’s time to overhaul the political fabric in Malawi we need to retire some names , we want something new, something fresh, a breath of fresh air …….,,do Tay Kalirani please sit down !!!!

Tizanka
Tizanka
5 years ago

Tay come grab your vote already king. Ndidzakuvotelani ankolo

Maliseche
Maliseche
5 years ago

Koma ku Malawi ndale zimaphweka, ndi awa omwe!

Mike
Mike
5 years ago

I would vote for FREDO, ,,,,,,,

Read previous post:
Blue Eagles Sisters defends MPICO Netball Challenge Trophy

Blue Eagles Sisters on Monday successfully defended the Mpico Central Region Netball Championship after beating City rivals Civo Nets by...

Close