Email a copy of 'Teacher wins in MCP primary elections in Mchinji West' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Teacher wins in MCP primary elections in Mchinji West' to a friend
A 23-year-old Malawian man was killed in a suspected mob justice attack in Johannesburg, South Africa Sunday and police in...
Congrats
heeeheede iwe rodriguas ukuti chani iwe….akazi ako sanakuwuzebe zoona kuti nawonso anayamba kumwa uwafunse akumasule pepa ndaulula pepa
NGAKHALE INE SI SAPOTA WA MCP KOMA NDINAKAKHALA KU DELA LIMENELI PANO NDITAMUVOTERA MPHUNZITSI KWA INE NDI GREAT ACHIVEMENT NDITHU TIYENI TISAPANGE KADUKA DZIKO NDILATHU TIKAMUVOTERE NKULU AMENEYU ZIKOMO
Koma adapanga chibwenzi ndi mzimai odawala matendawa(akumwa) wapaboma pa Mchinji, wakashop mumsika. Ndiye kaya!
Komanso tamvetsedwa kuti boma likusintha date lamasankho mpaka september, 2016. Ndiye tindalama tonse titheratu tsiku lisadafike. Palinso chikonzero chakuti afinye kasalary kamkuluyu, salandiranso mpaka kale kuti campaign imvute. Nanga titi kuchipani kutuluka saka lomthandizira. Chifukwa malinga ndi mbiri, zimavuta kuthamdizapo. Kaya kapena.
Izi tangoti zidziwike kuopera pamawa nkudzati bwanji sim’datiuze. Dzimvere.
as a public officer,Dpp is going to fire him very soon becouse he is from opposition.
komatu sikuti muziona ngati gwape ameneyi azawina ma by-election mwaalemba m’madzi
congrants Mr Mwale MCP motooooooo