Email a copy of 'Teachers Union of Malawi call off strike, wants heads roll at education ministry' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Teachers Union of Malawi call off strike, wants heads roll at education ministry' to a friend
Government is drastically cutting on its foreign mission staff with the first 20 recalled envoys are expected to jet into...
teachers kugona basi
WINA WADYETSEDWA CHIBANZI. KUMANGONAMIZIDWA BASI JUNE 30 MUKUWONA NGATI NDIPATALA LET US WAIT AND SEE. TUM OFFICIALS ATULE PANSI UDINDO NGATI BY 30 JUNE MAVUTO SAYANKHIDWA.
KUMANGONAMIZIDWA BASI.IFE NDIYE TINAYIYAMBA KALE.YANU YAMU JUNEYO IZANGOPEZELA.POKHAPOKHA MALIPILO AKADZAKHALA ABWINO IDZATHA.PANOPA ILI NKATI SITALAKA.
These people in government only listen when they are pressured. You want your rights, you need activism: strike, mass demonstrations, or something similar.
Amenewo ndiye aphunzitsi kugona kwambiri.
TUM IKULAMULIDWA KUTI:”OSADZATCHULANSO STRIKE” MUZILISIIRA BOMA KUCHITA MMENE LAONERA. TUM SIIDACHISEPO STRIKE YOTHEKERA
tum ur not serious strike cancelled why hav u answered /given wat u wanted if not some thing happened
This TUM is a joke. No wonder you guys(teachers) are tossed up and down like a ball by incompetent and corrupt ministry officials. Regardless, the strike needed to go a head as planned. That way the incompetent and corrupt officials at the ministry would perhaps engage an extra gear to sort out the made made administrative malaise.
Palibe kudyapo apa koma kuti they have to be patriotic.Nanga kukalipa kuja .
Game mwayitaya. mukalandira muzandifunse. Amenewo awopa kulepera kwa mayeso akubwerawa, ndiye mukangoti mwamaliza mayesowo, yizakhala nkani yinanso. You have been duped seriously.