Email a copy of 'Teachers Union of Malawi, govt talks start but flop: Strike on the cards' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Teachers Union of Malawi, govt talks start but flop: Strike on the cards' to a friend
Women police officers are increasingly facing abuses in their homes although they enforce such laws to other women in the...
Teaching is a noble profession. It’s more of a calling than a means to get rich. Ngakhale muwafunse ma lecturer makamaka a pa Chanco they know this. Kufuna kupeza bwino mungochoka monga mmene ndinachitira ine. Ntchito yophunzitsa ndi maitanidwe ndithu monga mmene amachitira Ambuye Yesu. Cashgate imavuta nanga munthu utani ndi chalk? Tabangophunzitsani basi.
Aphunzitsi Ndichani Kwenikweni,ngati Mukufuna Salary Yotchuluka Kapezeni Ntchito Ina,yamalipiro Abwino,musamatisowese Mtendere Ife,i Was Zea Koma Ndinazitaya,am Afreeman In The Freeworld
Strike mmmmmm i doubt ngati ine ndipanga nawo coz syllabus sindinamalize
Aaaaaah! Dont worry! Kuti ena afepo titumiza mphezi, timapanga kuno ku Tsangano. If we kill twenty TKs and TJs it means we have created posts for others, sichoncho?
If u r not teacher just b chete coz u dont know how painful teaching become when u r empty.Our TUM kpup.
ON THE PROMOTIONS OF PRIMARY SCHOOL TEACHERS, PLEASE MUWAKE TELL YOUR TEACHERS TO GO WHERE THEY ARE SUPPOSED TO GO, IN THE RURAL SETTINGS. AFTER ALL IT WAS AGREED AND WELL STATED IN THE APPLICATION ADVERT. GO TO RURAL AREAS IMMEDIATELY. OUR SISTERS AND BROTHERS ARE SUFFERING.PLEASE THE GOVERNMENT , COULD YOU FORCE THESE TEACHERS TO GO IN THE COUNTRY SIDE FOR TEACHING. TAKE THESE TECHERS HEAD ON. EVEN IN PRIVATE COMPANIES, YOU CANT ACT AGAINST YOUR EMPLOYER ESPECIALLY AFTER INTERVIEWS. AND ITS YOU MUWAKE WHO IS MAKING NOISE ON RADIO, WHY DIDNT YOU ATTEND EVERY IMPORTANT MEETING LIKE THIS… Read more »
Koma zomati promotion izikhalapo wina akafa ndiye zachambatu zimenezi,
Winayo afa liti? ndipo afa bwanji kuti wapangidwa promote asangalale?
Kodi Boma lakhala bwanji ili? kikkkkkkkkkk
Chifukwa cha umphawi munalephelanso kupita ku meeting poganiza ngati kuti Boma likakauonani nkhope akuthotholani pa ntchitoso eish koma abale!!!
you want to go on strike and yet you have children in those schools, mitu ikugwira pamenepa? why cant you give dialoque a chance
Teachers make huge contrinution to Malawi development, they deserve care and support. Govt must live up to its mandate in uplifting the lives of teachers.
aziphunzitsi ambiriwa samatha kuphunzitsa.