Email a copy of 'Telecom Networks Malawi invest $6.5m in modernisation program' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Telecom Networks Malawi invest $6.5m in modernisation program' to a friend
Local movie, ‘Mwayi Wotsiriza’ by Theatre International (TI) has received an impressive reception on Friday night at Golden Peacock Hotel in the...
Zikukhala ngatidi zikuyendako pano kusiyana ndi kale lija a TNN. Mumuchotse Mmalawi amene amayang’anira machine a dropped calls ukuyankhula. Ikaninsoni mmwenye pamplona pake. Mwachita bwino munalemba ntchito mmwenye kuti azikuthandizani. Kudzichepetsa kwanu inu a Chikaonda nkutenga anthu amakhungu ena mwasonyeza kuzama kwanu kwa risk analysis. Osamangolemba ntchito Mmalawi aliyenseyo chifukwa choli ati ndi kampani yachimalawi.Fotseki! Amalawi ambiriwa muno anabwera mayeso mnkalasi. Amakanika kunchito Koma strike amakhala Oyamba kutseka gate ndikuwavula abwana awo kabudula kuti malipiro akwere. UKO ku capital hill uko nde zatikanika. Aliyenseyo wokuba. Asiyireni azungu azitilamulira. Nationalism yatikanika. tnm ndi company ya chimalawi Koma inadziwa zofooka za a… Read more »