Whau our land has turn into a battle fied God come now to take me before it becomes worse.politicians are chamerions’thieves, and liars why my mother having problems cos of our stupid leadership
lne ndiye ndiyankhula basi a MACRA nambala yanga ndi imeneyi mumpatse Dausi akapeleke kwa bwana wake. posachedwapa ndinapita ku chipatala koma zachisoni anthu kumabwerera panado wachabechabeyu kusowa, odwala kumauzidwa kuti agule? ndalama azitenga kuti? ndiye inu a Dpp muli busy kumanga anthu chifukwa cha kuyankhula chilungamu?, dyera mtuni koma pasafike pa 2019. NOTE: ndakamba za Dpp osati boma mukafuna mulandu ndikakuyankha iweyo Dausi.
chochi
8 years ago
Welcome jelbin mk we missed you. Of course it is the two judges who actually sent Kabwila and friends to discuss regime change on whats app. They also caused hunger in Malawi. And they made your party to lose in the southern region. Shame !
anonymous2114
8 years ago
Freedom fighters? Are u crius…. They are getting bail nw wat if u do the demos are get arrested they will bail each other and leave u there. Am not a politics guy but ril guys all this is jxt politics it has nothing to do with other ppo suffering as long as they hav the power they are fine… Let’s stop listening to these politicians and build our own malawi , if this continues one day there shall b war n those suffering shall b us not them
Ahh! I don’t see any case here as former director of public prosecution. Treason? My foot. To hell with your charges. Ndiye bola akanamanga Gwanda chakuamba uja ankati alowa mtchire uja. CIRMS ija ankakana kuti akufuna kuti adziona zokambirana zaanthu ija ndimeneyo. Ndiye mutimanga ambiri. Koma mwati awa sadzimva zimene tukambirana kubedi. Koma Dausi eeee
patrick joseph sizala
8 years ago
i dont c any case/issue lets wait 4 de court 2 judge
brie
8 years ago
aaaaa ine nde sundikuona chomwe awamangira….
aaaa seriously? presidential advisors gv proper advice to ur bosss pliz,…..
mzungumbuli
8 years ago
Lets shun away from using Airtel numbers. Airtel ili ngati Yudasi iskariot idzakuperekani lets go for TNM guys.
JUSTICE KAMWANA
8 years ago
kODI PULANI MUKUPANGAYO NDI YA AMALAWI KAPENE MABANJA ANU. ZOMWE MUKUIKA PATSOGOLO NDI PHINDU LANU BASI. ANYAMATA MUKUWAFUNA KUTI MACHITE NAWO ZIWAWAWO AKAZAGENDA APOLISI PENA APOLISI NDIKUTOPA NDIKUWAOMBERA MUKUTANTHAUZA KUTI MUZABWEZELETSA MOYO WAO ANTHU OYIPA INU MUZIOPA MULUNGU NDALE ZAMTUNDU WANJI ZIMENEZO KOMA MUMAPEZAKO NTHAWI NDIKUMAPEMPHERA AKABWIRA NDI ANZANU GOD FORBIDE CHAKWERA AND YOUR PATY GOD CAN NOT ALLOW YOU TO BE LEADER OF MALAWI. TSONO MUKUONA NGATI PETERYO AKHONZA KUNGOKHALA PHEEE KUMATI MWAPANGA TIMAGULU TANU TOLANDA DZIKO ZOONA MAPETO AKE MUKAYAMBA KUBWEZELANA CHIKHALA CHANI SINKHONDO IMENENEYO. ZIMENE MUKUKAMBIRANAZO MAFUMU AKUKUZIDZIWA NANGA ENI DZIKO AMALAWI AKUZIDZIWA KUNOTU SI KU EGUPUTO… Read more »
Whau our land has turn into a battle fied God come now to take me before it becomes worse.politicians are chamerions’thieves, and liars why my mother having problems cos of our stupid leadership
yayi odala msatero okumanga,wanthuwatu soluchedza ukwidzinga