Email a copy of 'Three suspected thieves burned alive - Malawi Police' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Three suspected thieves burned alive - Malawi Police' to a friend
Former Malawi national football star Chiza Nyirongo has proposed Football Association of Malawi (Fam) to consider hiring Flames legend Lawrence...
Ndiye njira yokhayo yothanilana ndi Mbava, akagwidwa Kumangoyatsa Moto basi. Apolice ndiyeso akupanga umbava zedi pa Malawi pano.
apa ndiye ziri bho! munthu wina wavutika kuti apedze kangachepe basi wina ngwangubwera nkusomphola yayi dere apapa ndikuti congrats ma guy nonse munatengapo mbali potentha vimbavavo! nawe rhoda manjolo; anzako akuphedwa general public yati ithandize ukuti yayi next adzadiwitsa iweyono! ife mafumu athu anatiudza kale once mwakola mnkhungu komani waka kuluta nayo ku polisi cha chifukwa tikuvwirika cha andiso ena mwa mbavazo ndi apolisi amene. tithana nanu mpakana muzasiye
Woyenda nd lupanga……………….aaiwee! ee! Waziona lero.
Zilibo pamalawi?tizingophana
Jesus said to the people IF anyone of you have not sinned go ahead and stone this woman.
Mwawapumuzako apolice,nao ndi anthu amalema.Ngozi panseu apolise,anthu akhapana uku ndiuko -apolise!!. Amatopa ka. Thanx ana agogo chalo Mwanza for job well done.Kalonga, kuluunda komanso ma T/A ena, mwaona chitsanzo chabwino, osamachedwa nazo izi-so long umboni okwanila ulipo.
Congrants.
nde’bwino kwatero chifukwa aeniake aziwetozo akanapusa akanaphedwa!
usiseme wezi, sema nyama choma !!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
THIS IS NOT ENOUGH. TIZIPHA AT LEAST MBAVA 10 EVERYDAY. BY CHRISTMAS TIME WE WILL BE CRIME FREE.
ZOFUNA