Email a copy of 'Times TV Suspends Blak Jack for soliciting ‘bribe’' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Times TV Suspends Blak Jack for soliciting ‘bribe’' to a friend
An Egyptian investor has launched an executive bus service called Blue Bus that will operate between the cities of Lilongwe...
waba iwe…waba iwe….nanga waba ndani zimenezizi…nanga waba ndani kumenekuku…kkkkkkk koma blak jack eeeeesh ai ndalama wavuta pa Malawi kkkkk…
Ife we knew kuti mkuluyi sakhalitsa kuba too much even ku secondary ku mulanje amaba zedi uyu kape…wataya bomwetamweta
Kodi simungaikepo ena kuti ku LL kuno tiyambeso kuonera T. TV.
Kodi dimungaikepo ena kuri ka LL kuno tiyambeso kuonera T. TV.
Employ the right people. This guy has a problem.
hehehehehehe eishhh ukatambatamba uziyang’ana komwe kuli dzuwa….kodi mwambi umenewu simunamvepo?
ngwakuba ameneyu kkkkkkkkkkkkkkkkkkk haahahaha
TimesTv sikuoneka ku lilongwe
Zona bwanji
Lol….eh koma adha …ma tv personalities awa ayayayay