Email a copy of 'TNM to unveil new Malawi Super League trophy: Lucius Banda gig at Bullets, Mafco re-launch match' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'TNM to unveil new Malawi Super League trophy: Lucius Banda gig at Bullets, Mafco re-launch match' to a friend
In a rare spirit of sportsmanship, Mighty Be Forward Wanderers and Mafco FC on Wednesday, September 9, 2015 trained side...
Basi kumalawi ndinchoncho
Big bullets woyeeeeeeee big up gys…
Big game indeed a must win for the people’s team but chaphunzitsidwa or the double crossed sword soccer instructors are a force to not to underrate them
Ok!
How many times are u going to launch the same league during the same season ??? That’s why malawian football keep on going down due to the Britons of our leaders in sports section..
Ma models akadyetse ku Lakeshore.
Zili boo but sir mmm akula why not mablacks with kuimba ten?
Model Koma phazilo fanika chizilo
Good news but the venue is not good poor turnup for spectators which results in low revenue to be collected. With Sir Lucius Banda performing the re-launch would have been in any of the cities to pull huge football lovers ndiye kuti ife mapalestina tikanadzadzitsa stadium uku tikudziwa kuti tikuthandiza team yathu. Anyway poti siine Gomezgani to dictate match venue
Kodi abale azanga tandithandizani ndi leaue iti tinamvapo kuti akuchita launch?nanga ndi league iti yomwe amachita launch first round/second round amalawi tizichenjera apa ndipodyera ndalama anthu mwakhala mukulira kuti ndalama zikuchepa koma lero ndikudzeni kuti ndalama zamaonongeka munjira imeni if u look @ 95m ndi ndalama zambiri koma owina ndi 15m ndipo 80m ikuthela admin zoona zimenizi? ndalama ndiyambiri koma ma launchwa ndi momwe ma marketing managers amadyera dollar………..EPL/LALIGA/BUNDAS/ABSA KULIBE ZA MA LAUNCH……