Email a copy of 'Toilet turned into a teacher’s house in Malawi' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Toilet turned into a teacher’s house in Malawi' to a friend
Malawi Police in Dedza Monday morning shot dead two armed robbers for trying to hijack a car and third suspect is battling...
Zochitika Ku Mw.
Ndizomvetsa chisoni.Dele a kuedu. mukamava zimenezi chakudya chimalowa bwinobwino kukhosi kwanu,nkumasangalala?ntchito yanu ndikusokoneza aphunzitsi pa ntchito yawo?
The govt is full öf stupid ministers especialli minister of edu.
Koma sala ndiye kuphunzitsa ku town munakufunatu. Mpaka mthoyaz!
Wamisala osagenda kkkkkkkkkkkk!!!!!!!!! Ndiye mukuti ndikamchimbuzi?
Misala ilipo yamitundu mitundu mphuzitsiyu akufunika check up
Sikuti nyumba zikusowa, nkhani ndi yakuti amalandira ndalama yochepa , yoti sangakwanitse kulipira lendi ndi Transport kuphatikizapo zinthu zina zofunika pa moyo wamunthu chifukwa akanatha kukakhala kwa kachere, kubangwe , BCA, Ndirande , Machinjiri mix makhetha, chilobwe ndi kwina pongotchulapo madera ochepa, kodi chimbuzicho chinasiya kugwiritsidwa ntchito liti? chifukwa tikhoza kumangoti ndi chimbuzi chitasiya kugwira ntchito nthawi ya Kamuzu .
Kodi komweko kulibe school commitee?Kumadalila boma zilIzonse mapeto ake ndiwomwewo.
I feel sory 4 my nation. I think u leaders u r taking full advantage of us bcz we r poor. But knw that God sees us and will let us pass through these kinds of stituation.
Mbyofo mbyofo Pitala is wasting time sign some graffiti in Lumbadzi corner and painting filthy corner in police cells while teachers are sleeping toilets.All those allowances would have built a modest house for such a poor soul in such an unappreciated profession.Shame indeed.