Email a copy of 'Two Malawi police officers arrested for robbing Zambian woman' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

29 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
mnyamata oyikonda nyasatimes

FOR YOUR OWN INFO. KU ULIWA MAFUMU ANALAMULA ANTHH AWO KUTI ONCE AGWIRA WAKUBA ACHITE NAYE MUMENE ANGAFUNIRE BUT SHUD NEVER TAKE AKUBAWO KU POLISI CHIFUKWA ENA OMWE ALI NKUBA NDI APOLISI AMENE! I REALLY LIKE THIS ! WHY CANT MALAWI INTERODUCE SHALIAH LAW! OR SHOOT TO KILL!

piksy
piksy
8 years ago

atuluseni

Akatswiri
Akatswiri
8 years ago

The possession of game trophie is an offence ,let the Police officers free and again the woman is also involved in corrupting the officers.

Penjaninge
Penjaninge
8 years ago

Anyöngedwe

quincy majawa
8 years ago

Padusanso chinyengo pamenepa,chifukwa chani m’mayiyonso sanamumange?chifukwa apolicewo sanapite kunyumba kwake ndipo ndalamazo anawapasa ngati ziphuphu kuti amusiye,apolice akunchinjiwo mayiyo waangwirisa chinachake.

ndaona
ndaona
8 years ago

Ngati ndalama zikuwachepela a police wo osasintha career bwanji? Ndani samadziwa kuti mboma mulibe ndalama? Zonse abazo bwanji osadzilipilila school? Langison ku Limbe police ndi wakuba kowopsya, plis deal with him afufuzidwe. Alwas kwa kachere kubera anthu mdzina la police, timukazinga msiyeni.

mgoni
mgoni
8 years ago

Nthawi yonseyi takhala tikuvutika not knowing ndi a police athu omwewa amene akutivulaza. Onse a police pa malawi pano amacheza ndi mbava no wonder samagwidwa akaba akubawo. A man was killed in BCA and the police arrived after 2 hours. The robbers snatched the rifle , a licencd one from the deceased koma mpakana pano siinapezeke. Timve zenizeni

PATERO
8 years ago

WHY POLICE SPOIL YOUR NAME MONEY NOTYOUR US U DEMAND RESPECT YOUR WORK ROB PEOPLE NOT GOOD NOW U R IN JAIL WHY NOT LOVE YOUR WORK U LOVE MONEY

kelvin Mahomed Spiece g
kelvin Mahomed Spiece g
8 years ago

anthu oipa inu…akawalala ,askaweza …mboli xanu ‘panyini panu…dzulo mwandimenya kwambili..ndepoti ndaxiwa kumene mumakhala nose ndikupexani…aFisi inu…Mapwala anu Nonse Ku Police ko

muxingo chita Ngozi simuma nyela mwano
Choncho
.

Vakabu ya amphawi.
Vakabu ya amphawi.
8 years ago

Apolice ndi akuba komanso opanda chisoni, mbava akulephera kuzigwira chifukwa amabera limodzi. Ndiye ati pofuna kuwonetsa kuti akugwira ntchito akumapita mma bar amene ayiniake ndi osantchuka ndikumakagwiramo anthu okumwa mowa . Akatelo aziwakolopora dolla ati adzipulumutse. Kodi vakabu yanuyo bwanji simumakagwira ku Chez ku Sterio kapena pa station olo new casabulanca? Mumafuna kuwabera anthu osauka podziwa kuti alibe chilichonse sangakutengereni ku court. Olemera mumawawopa. Vakabu yanji yongogwira anthu oyenda pansi okhaokha koma ammagalimoto ayi? Apolice okuba inu mumangana simunati.

Read previous post:
M’methiwa school benefit from TNM’s Ufulu promo

M'Methiwa Primary School in  the area of Traditional Authority Kapichi in Thyolo district  has become the latest beneficiary of TNM’s life-changing Ufulu@50...

Close