E-Mail 'UDF dismisses ‘anonymous’ petition as works of detractors' To A Friend

Email a copy of 'UDF dismisses ‘anonymous’ petition as works of detractors' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
Please share this Article if you like Email This Post Email This Post
  Subscribe  
newest oldest most voted
Notify of
cocobe
Guest
cocobe

Atupele,to win election,its not about money koma umuthu.ulinao umuthu?UDF kuzikonda,ndakhalamo ayi naneso ndazituluka.tidali ndima MP ochuluka,pano number ikungo sika nasika.nde kaya umazifusa?khala naka kachipani kakooo kanyumba

jack mamedi
Guest
jack mamedi

u hav failed mr hon.Atupele oooooooo no no no no.zikavuta timangovomereza.sungakhaleko ngati Hon chiwaya?satengeka komaso amaganizila athu amene akungwira nawo nchinto.apa nde chipani chatha chatha.kanyuka nduuyo mwanchosayo,chifukwa amafufa kuti zikuyenda bwanji.lero mwanchosa.paja mumafuna ma yes bwana.nkozomba angakuuze chani sibolani zake zikuyenda.pano nde ndakwereretu ya chakwera.

paul mwanaveee
Guest
paul mwanaveee

inu abale kodi muthu ngati uyu angati thandize?kodimoti akamakhala amaonangati angazawine?akunamatu ameneyu.afuse ose amene akhala akungawa chifukwa samava ngati iwe.tuluka paja ufuse fuse kuti athu kujaku akuti chani?olo bwana Peter muthalika atati akupase u president sungawine.olo atati uyimile DPP mapeto ake ma MP ukhoza kupeza 5 komaso iwe kuluza.

zebede
Guest
zebede

tiyeni azanga a UDF tinene chilungamo.Atupele wationjeza,atupele satha kuganiza payekha.ukafuse nkozomba,Ajera akangoti ayi ndi ayi muthu akangoti wadana ndi ajera ndekuti zako zada.kaya zinali zakunchito aaaaa,nanji zachipani ndenanji Ajesoo the great.chilichose ndi kozomba & ajeso the great,gati ajeso anathamangisisa P.A. wa Atupele ameneso anali bale wake[Imran] cholinga Nkozomba aziyendesa bwino zimidala za ajeso.koma eeeeee chaka chake nchino.Imran analakwa chani.nkozomba wapanga zingati kuba ndalama zambiri koma alikuti?chifukwa sucheza ndiazako vuto ndilimenero koma amwenye oooooooooooooooo,yaumeya inkhoza kukukhaladi.Nowel chalamanda amapanga zaku office ndizaku office. Hon.Minister chalamanda muphuziseko nchito mwanayuuuu.pliz,pliz’pliz

Imraan Sadick
Guest

This petition cannot be taken seriously,he/she should have criticized under one’s noise not while wearing balaclava ,without a shadow of a doubt this is a brainchild of PP,it sounds more more like them
UDF believe in unity-we have to unite if really our country is to develop`UDF is very conscious of the development`
it’s
basic truth people rejoice when other people are fighting and vice Versa-mukunva phain
And for the record Munthalika administration is not to blame for the economic crisis Malawi is going through,the blame should be directed to Joyce Banda and her accomplices
Munva mmimba simunati
Atupele Woyeeeeee
Peter Woyeeeeee

Mchawa
Guest
Mchawa

Ken Ndanga is a puppet, pompano amalira kuti palibe chomwe akupezapo anavutika zedi nthawi ya campaign, lost energy, samadya mokwanila koma palibe compensation ina ili yonse. Anthu a UDF ndi zitsilu amakanika kupanga criticise Atupele for fear of being removed from the party. Problem UDF is financed by Atupele and his father that’s why the members does not have a say. UDF is a family party and does not belong to the people. It’s high time the UDF leadership strategized to get other means of funding or else mukhalira kulila ndi kukukuta mano. Atupele akuzunguzani mutu nonse mukhala ngati opanda… Read more »

Chejumo
Guest
Chejumo

Atupele is clever and for choosing to work with government that’s being patriotic. Leaders are there to serve the people. Him as President should serve the interests of all Malawians not just UDF party. Unakhonza Atupele. I am just worried that you are becoming a recycled politician. Jumping from one ship to another. PP unali mommo wadyako, yabwela DPP uli komko. Not sure if you could be able to criticize recycled politicians come 2019.
I salute Chiwaya samatengeka.

Wapa Monkey Bay
Guest
Wapa Monkey Bay

LUCIAS BANDA has a guilty shocked with Atupele of his acceptance to be one Cabinet Minister without proper causatations to the members of UDF thats why Hounorable Lucias keeps quiet of not commenting issues related to DPP. He is not happy at all.

Uthmaan Abdullah
Guest

AT LEAST MR AAM, BRIEF MALAWIANS ABOUT THIS PARTINERSHIP.

Arthur G.M. Mtambo
Guest

BE CAREFUL UDF, THE PART WILL PERISH OR END UP LIKE AFORD.

CHISOMBA CHIMENE CHINAMEZA NOAH, CHIMEZA UDF, KOMA OSATULUKANSO