Email a copy of 'UDF replaces poll committee, party primaries set next week' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

3 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Munthu wa Mulungu
Munthu wa Mulungu
5 years ago

Tiyamikire udf poiwonera patali komiti yawoyo. Ku MCP mpakana pano zinthu zikuvutabe. Mchinji ibetsa mipando yosachepera itatu ya aphungu chifukwa cha mapulaimale ochitika mwachinyengo. Mpakana pano zotsatira za madera anayi mwa madera 6 sizinalengezedwe ndi election commit. Zina akuuzana mwachisinsi. Kaya, zioneka. Koma Mchinji central yokha ndiye zanyanya. Simungalengeze zotsatira pomwe mavoti sanawerengedwe or kusainira. Chipani chiona zakuda 2019.

Honourable
Honourable
5 years ago

fulumilani nawo ma primaries ‘wo enafe tikufuna tiimile nawo..makamaka ku BT West constituency

Shitholes Diarrhoea Progressive Party

Udf? What? Chipani chatha ngati nsalu ya makatani. Ndikuti kumpoto? Chatha. Nanga pakati? Chatha chatha. Olo atanditira dumu nkamwa…………..

Read previous post:
Comsip restoring livelihoods with enhanced savings, investment knowledge

The Roads Authority with funding from the World Bank is reconstructing the 46 km Karonga-Songwe Road and the project has...

Close