E-Mail 'Uladi, Msonda contradict on PP coalition with MCP' To A Friend

Email a copy of 'Uladi, Msonda contradict on PP coalition with MCP' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
Please share this Article if you like Email This Post Email This Post
newest oldest most voted
Notify of
chikhalawaka
Guest
chikhalawaka

UDF siingapange mgwirizano ndi chipani China,come 2017 muzamva kuti atupele wachoka kkkkkk cifukwa iyeyo afuna u president,osaiwala kuti mkapanga mgwiridzano ndekuti atupele vice president mwayiona zomwe chilima sangalore,ndipo kungochosa chilima akapangitsa kuti MCP iwine think twice

mijomba ikuluikulu
Guest
mijomba ikuluikulu

MCP ndi PP mwayambayo ndi misala, inu munamva ndani kuti njobvu amaimangira mpanda kapena khola? Chomwe tingakulozeni ife a DPP eniake a boma /dziko lamalawi ndikumalota mukulamulira dziko linalake osatiso lamalawi ayi.Ndipo kuti mudziwe kuti ife a DPP ndi akatakwe pa ndale ,pofika kumathelo achaka chamawa tizakhala titakulandani mizati ya tizipani tanuto kuti muzadziwe bwinobwino saizi yanu.

Vwapuvwapu
Guest
Vwapuvwapu

Wait and see kkkkkkkk.
Umapambana ukadutsa malire kkk

Ine wa Titus Scot
Guest

My brother Titus Scot, people think we southerners are stupid come 2019 it is us to boot out Peter. They have forgotten our APM got the presidency last year when DPP was just a mere party after the demise of our Great Moya Bingu. In Phalombe we have all agreed that come 2019, it is APM,APM,APM,APM,APM,APM! APM boma 2019. DPP boma 2019!

Peter Mathanyula
Guest

Dpp will triumph in 2019 through vote rigging as it was in 2014. For your own information if this happens Malawi will be worse off than today and Dpp supporters are happy with this kind of condition. Sorry.

levelheaded
Guest

Chimene DPP simudzaithera Ku Malawi kuno ndi chifukwa choganiza mopelewera anthu a Ku opposition. Zitangotuluka zisankho za 2014 next move ya opposition was to form the grand coalition comprising MCP,UDF,PP and all other small parties but instead munachedwa ndi kuliralira mma radio ndi mma news paper kuti eeee atibera mavoti, pamenepo mkuti the mighty DPP ikuganizira zodzawinanso 2019 mwansangansanga mkupanga mgwirizano ndi UDF . Lero za mmbuyo mwa alendo basi ng’weng’weng’we tipanga coalition,kkkkkkkkkkkk. Ngati mumalira nayo yokha DPP ndiye pano yawonjezera eastern region yonse under UDF ndiye mukulotabe zodzatenga boma 2019? Ataaa, maloto a chumbatu. Dikirani mudzalirenso 2019. Zodiak ikangoti… Read more »

SONG
Guest
SONG

The mathmatics is simple here achimwene DPP+UDF VERSUS MCP +PP. Lets add up votes of 2014 elections. Who wins here. Anthu inu a DPP ndinu zitsirudi because peter got 36% MCP 28%, PP 21% and UDF 13% this gives a coalition totals as follows, DPP/UDF 49% while MCP/PP 49%. Therefore we need rerun to get 50+1% votes. Peter is not popular in this country and can’t beat Chakwera I repeat can’t beat Chakwera twice particularly if u merge with UDF Chipani cha njala you are gone guys. We are drinking wa Mkaka 2019 stay tuned.

Usafunse Yankho
Guest

Tsogolo La Dziko La Malawi Mulungu akudziwa motero mawu msamatha musapusitsidwe ndi masankho apita popeza mavotedwe omwe achitike mu2019 ndi osiyana ndipo ambiri sadzakhululupirila zomwe zidzachitike.Tisagamule poti zipani zonse ziri mMalawi atsogoleri onse ndi adziko lomwe lino

Willie Chimseu
Guest
Willie Chimseu

wishful thinking

Happy Eduardo
Guest
Happy Eduardo

Worse still mgwirizano wake nkukhala wa PP ndi MCP. Does PP have a political base in Malawi? MCP does not exist in the South while DPP and UDF do exist in the central and northern regions. Search me.