He was prosecuted for stealing money from client? Koma misonkho yathu idzalimba? Izi ndizomwe tikukana,munthu wa mbiri yoipa ife takana.
Stainor Maonga
8 years ago
Kodi zipani mukufuna zikhalepo zingati? Simple arithmetic: the population for Malawi is 17million against 35+ parties = >2million. zonsezi mukufuna maudindo, kusokoneza kapena kutchuka? abale anzanga, zipani zachuluka. USA is very rich but how many parties are there? Tsopano pakhale lamulo loti ngati chipani sichipeza mpando, chichotsedwe pa mndandanda was zipani zobvomelezeka.
Tapulika.
Kadakwiza
8 years ago
Selfish leaders. Malawi don’t need another new political party. What Malawians need right now is revolution to get rid of these selfish leaders who have made us Malawians suffer. If Mr Shawa want to Malawians let him join the already existing political parties. Mr. Shawa will not help.
KOMA ATOLA NKHANI ENA ZITSILU BASI..KUDYA MABAZI BASI…KUFUFUZA BWA? UP! UP! UP!
TISAMUSIYE AMENEYU..AZOLOWERA
Starling Kondowe,Chikwina CDSS in Nkhatabay
8 years ago
Parties have emerged with a lot of manifestos.To my surprise not any of these parties have said a new thing.Their tune is just the same with incoherences here and there.I beg these political titans,to stop forming new political parties,but formute strategies that can be used in tackling problems which our country is facing.
mzomera wa mzomera
8 years ago
I am in Zomba count me in Mr shawa I will support you more [email protected]
He was prosecuted for stealing money from client? Koma misonkho yathu idzalimba? Izi ndizomwe tikukana,munthu wa mbiri yoipa ife takana.
Kodi zipani mukufuna zikhalepo zingati? Simple arithmetic: the population for Malawi is 17million against 35+ parties = >2million. zonsezi mukufuna maudindo, kusokoneza kapena kutchuka? abale anzanga, zipani zachuluka. USA is very rich but how many parties are there? Tsopano pakhale lamulo loti ngati chipani sichipeza mpando, chichotsedwe pa mndandanda was zipani zobvomelezeka.
Tapulika.
Selfish leaders. Malawi don’t need another new political party. What Malawians need right now is revolution to get rid of these selfish leaders who have made us Malawians suffer. If Mr Shawa want to Malawians let him join the already existing political parties. Mr. Shawa will not help.
what do u gain when you insult atumbuka? Agalu enawa kkkkkk
what do you gain mukatukwana atumbuka? R u so special before God?
ZOPUTSA BASI TATOPA IFE NDIMA Briefcase Parties.
Zipani zachuluka izi ndalama zanuzo bwanji osathandiza amene akuvutika ndinjalawa bwanji?