Bwanji osasaina food agreement.Akudfuna azitenga military yathu nkumagwiritsa ntchito ku Liybia,Egypt ndikwina komwe ayamba kuphulitsa
jolozakapokola
8 years ago
Tiyeni nayoni Tayifa basi….atimalize ndi njala yathuyi
gabro
8 years ago
The USA is looking for partners(no matter how small) in preparation for World War 3 which gathering momentum every passing day in Syria. Russia is not ready to pat on Obama’s back. Just wait and see!!
Nangantani
8 years ago
This is dangerous. How can you sign a security pact with an enemy. Mai uyu anali munyuzi posachedwapa kuti akuyenda ndi adani a boma. Lero nkumagwirana naye chanza pamene anzake amene amapanga naye za upandu tawamanga. Bwinotu bwino. A Dausi mukuti bwanji pamenepa. Masewera sapanga pa ulimbotu. Mayi ameneyu apatsidwe 48 hours azipita kwao basi. Ifenso nzungu wathu uja alikwaoyu azibwerako tidzaonere limodzi mabvutowa. Komanso ana a bwana aja azibwera tizadye nandolo limodzi.
mahada
8 years ago
Police ndi deal cz of being daily active on ground
Mai a Farai
8 years ago
Kodi why Chaponda not VP or defence minister?
Buyelekhaya
8 years ago
Mwaona a Chaponda tsopano!
His Excellence the Life President Wolemekedzeka Mkango Lion Chivomerezi Chisokonezo Artillery ArchMissile Manthakanjenjemereza
8 years ago
GETTING MILITARY ASSISTANCE FROM THE SAME PERSON WHO WANTED TO TOPPLE GOVT. THIS GOVERNMENT NEVER STOPS TO AMUSE ME. KKKKKKKK!!!!!!
Fabiano
8 years ago
GETTING MILITARY ASSISTANCE FROM THE SAME PERSON WHO WANTED TO TOPPLE MALAWI GOVERNMENT. KKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKK!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!!
BOKHO
8 years ago
Where is deputy minister of Defence. A Chaponda bwanji kuufuna u president. Stupid MDF was brought up by Kamuzu all that discipline and professionalism u see a leads bambo.