Email a copy of 'UTM condemns Aford violence on Mwenifumbo rally' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'UTM condemns Aford violence on Mwenifumbo rally' to a friend
Malawi Police in Mangochi District on Thursday pounced on one of the UTM Party presidential campaign member Al-Haj Ben Kambulire...
Komanso timanvako kuti some women were undressed Aford cloth, why is this issue suppressed? Aja mumapanga ma demo aja mulipo? Kapena simudamve? A Kabwira kapena mwabwira shuga and you are unable to speak? What’s up?
Once a thief always a thief now Mwenifumbo wants to steal AFORD identity. A thief remains a thief for life. No shame no honour this man Mwenifumbo.
Mwenefumbo ali ndi ntima wonyasa, wantopola. Munthu pagulu supanga za wekha osafunsa anzako. Ali ngati wina uja wa ku MCP. Mumakhala ngati wodya drug.
UTM better behave izi ndindale mumanena a DPP now its you guys. Osamadalira kuti atsoleri anu azingopepesa no we shall not accept that.You need to walk the talk
Wamvapo zoti a UTM ndi omwe amachita zipolowe?? Sumatha kuwerenga nkumva chizungu kapena eti! Read and understand before u open ur mouth.
They are bed fellows with aford nfati sizikuwakhuza bwanji chidanti akupepesa .You hv to look at the bigger picture mbuli iwe eti?