Email a copy of 'UTM in ‘clenched fist of truth’ to defeat propaganda' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'UTM in ‘clenched fist of truth’ to defeat propaganda' to a friend
A whooping K3 million is up for grabs this afternoon as the K35 million Gateway Central Region Netball League Challenge...
Utm singazizile chifukwa chainu ma cadet , muwanva kuwawa a utm motoooooooo buuuuuuuuuu, muziwaso ameneuja CSK ma cadet chinto yanu tikuiziwa sife ogona
UTM moto wayamba kuzilala mapesi onse atha kuyakha what remains is phulusa basi shaaaaaa!!!!!!
What is utm?A company,NGO or what?Chilima wanyanyala wakusiyila kaliati ndi masangwi wakoyo,,,,convention pa November Kodi mwalembetsa liti?Mukutaya nthawi yanu pachabe Chilima sazayima pachisankho,,,,kkkkk
A Noel Masangwi adatsogolera anthu amene anapha mnyamata wa sukulu ku Malawi Polytechnic Robert Chasowa. Mpaka lero a Masangwi ndi gulu lawo kuphatikiza a Peter Arthur Muthalika omwe anali nduna ya boma nthawi imeneyo sanayimbidwe mlandu. Ngati a Chilima ali ndi chilungamo akanaonetsetsa kuti anthu amene anapha Chasowa alangidwe.
Please leave out Manganya in this. He should concentrate on what he knows best: TIKUFERANJI. Have you noticed of late how dull his Tikuferanji episodes are? Utsogoleri requires seriousness.
Band yagawana zida apa basi kkkkkkkk. Munya muona
A Secretary General amene amalankhula without thinking according to Mayi Calista Chapola. One whose education is little . Very strange to hear kuti anthu asiye kutukwana during political rallies, and yet akweni is number one. No wonder Calista calls her one who speaks before thinking. Please try Manganya as you leader and leave it chidakwa chanucho if you are to leave a mark in Malawi politics. SKC has failed you all.
UTM ,you have got a big task ahead of you with this poor attendance rallies you are addressing!Muziona ,ndale simasewera and more especially to convince rural folks to change their party allegiance to new ones.
Mwagwa nayo apumbwa inu, UTM moto kuti buuu. Walira mokweza cadet.