Email a copy of 'UTM running mate barnstorms Mangochi: Usi decries under-develpoment' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

20 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Malamula
Malamula
5 years ago

Ife Achiyawo mmene zafikapa timati Ayishoshe alikonye, UTM Wooooooooyeeeeeeeeeeeeee. Wina azathawiranso kunja chaka chino , maskafu paphewa , kodi simuona kulemera < Aaaaaaaaaa, zovuta kwambiri.

Malamula
Malamula
5 years ago

Zikomo a Malawi anzanga, ndasangalala ndi anzanga akuno ku Mangochi , kumeneko ndiye kubwera. Funso langa madzulo ano ndiloti : a DPP akumanena kuti tikampeza munthu wogulisa Achialabino timugwire ndipo atiululire kumene amagulisa kapena amene amagula anthu amenewa , kodi anthu amane anawagwira kale osawafunsa iwowo bwanji ? Nyuzi yalero pa 22/03/2019 mwalembedwa nkhani yoti bambo wina wamangidwa chifukwa chofuna kugulisa mwana wake , bwanji osamfunsa amaneyo kumne ankafuna kukagulisa mwanayo. Inu ndine tikanena kuti amane akugula achialabino ndikuwadziwa , azatimanganso , kwenikweni chimene a DPP akufuna ndichani ? Malangizo anga kwa inu a UTM , musalimbane ndikupanga kampeni mtauni… Read more »

McDonwell Makuwila
McDonwell Makuwila
5 years ago

Your VOTE, your CHOICE, your VOICE

Ankhwinda
Ankhwinda
5 years ago

Pitilizani lmbizo pang’onopang’ono mukuwayandikila anthu akumudzi ndi zomwe zikufunika osagwa phwayi nthawi yatha iyi

namatetule
5 years ago

Problem is that Ayao kubelekana kwambiri so izi sizingatukula mabanja or district or dziko. Everyday they worry what to feed 15 children let alone what to dress them- asanaganize zowatumiza ku school

JCInLA
JCInLA
5 years ago
Reply to  namatetule

Namatetule, iwe ngati m’Malawi, kuyankhula ngati kumeneku sibwino. We need to respect one another. If another group is breeding more than yours, then this is not your personal problem. You don’t feed any of them.
I can be of any tribe, however, I am a loving Malawian who grew up with Yaos, Tumbukas, Ngoni, Lomwe, Chitonga and I respect them all. So, I urge you to go back to your village and ask your mama or papa to teach you properly before leaving your little town.

UTM Boma
UTM Boma
5 years ago
Reply to  JCInLA

Tamuuzeni, sadziwa kuyankhula

Mirella K
Mirella K
5 years ago
Reply to  JCInLA

Ndipo which Mtundu subelekana kwambiri ku Malawi? How many are Chewas and Lhomwes compared to Yaos? Zauchitsiru basi

Moni
Moni
5 years ago
Reply to  namatetule

Chifukwa amakoma, mumati a zii ngati inu mungabereke?

Amgwagwa
5 years ago

UTM!!!!! Ndatitu UTM!!!!!!!! BOMA ILOOOOOOOOOOOOOOOOOOOO

Necessary Noiz
Necessary Noiz
5 years ago
Reply to  Amgwagwa

Kuti bu!!!!!!

mulumuzana
mulumuzana
5 years ago

we from UTM are not seeking another chance for most of these politicians are seeking another chance.tikudzakonza nyansi zonsezi…ngati mwalemba anthu awiri ntchito …wina otsogolera ndikumamutuma nzakeyu, winayo otumidwa basi…nde pazifukwa zake utumai waleka kumutuma otumidwayo koma inu mukuwalipila malipilo awiriwa…..kodi olakwitsa pa awiriwa ndani???tsono chaka chino tingochotsa otumayo ndikumupatsa mphamvu otumidwayu basi….tikufuna anthu oti akatigwirire ntchito osati anthu oti akuzimva ubwana namawina zisankho zisanachitike…ndamvetsedwa kuti ku mangochi konse nonse mwadzuka …zikomo for keeping it UTM……U T M moto moto moto kuti buuuuuuuu

Linda
Linda
5 years ago

Tianthu 10 basi

kavibangwa
kavibangwa
5 years ago
Reply to  Linda

zakuvuta linda uzimangirira chaka chake ndi chino hahahahahaha

Amgwagwa
5 years ago
Reply to  Linda

Iwetu zikuvuta!!!!heheheheheheheh mmasomo udayamba khungu ati!?

Mbagwezi
Mbagwezi
5 years ago
Reply to  Linda

The message is still going across Linda

Necessary Noiz
Necessary Noiz
5 years ago
Reply to  Linda

koma umaziwa kuwelenga iweyo?

Patrick Mbewe
Patrick Mbewe
5 years ago
Reply to  Linda

Hehehehede ulu. Ma fone a china manje akudula ma picture. Zovu zedi
Linda AKA Ben Phiri wabweranso pano,? Kumasuzumula zoona

Mr Malawi
Mr Malawi
5 years ago

UTM boma…wake up malawians enawa awa angofuna maudindo they dont wish good malawians

UTM Last Born wa DPP of UDF
UTM Last Born wa DPP of UDF
5 years ago
Reply to  Mr Malawi

Tell yourself that

Read previous post:
Fake Malawi presidential ballot paper sample in circulation

Malawi Electoral Commission (MEC) has said there is a fake presidential ballot paper  circulating on social media and has asked all...

Close