Email a copy of 'UTM storms Salima to tout Chilima’s presidential bid' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'UTM storms Salima to tout Chilima’s presidential bid' to a friend
The Catholic Commission for Justice and Peace (CCJP) of Karonga Diocese has said Karonga District has a long way to...
game on Chilima and Chakwera were ta Mtendere Secondary School. But the problem with Chilima is Kaliwo and Richard Msowoya. These two will confuse the party or the movement. They left MCP simply because they did not want Mia. Msowoya is very selfish. Them a wolf in a sheep clothing.
Musamuopseze munthu er
Mavuto tili nawobe basi….
KKkkkkk zowana sofula
Saulos Chilima, before launching your UTM, ask Brown Mpinganjira what happened to his NDA party.
And youthful president Atupele. Anthuwa ndi ma DPP disgruntled members.
Tiyembekezere kusintha ndi masangwi,katiali, loveness Gondwe, ngumuya.
Chilima anabera ma vote 2014 kodi ife a MCP tingamuvotere?
Sungafanizire NDA ndi UTM,Chilima ndiwachikulire
Weretethe ukunama kwambiri. UTM & NDA chimodzimodzi, bolanso NDA chifukwa amadziwikako m’midzi komanso inayamba pakanthawi osati UTM imene ikuyamba mawa mawali pa 21 May 2019 kutatsala miyezi 8 kuti anthu avote. Mwachedwa nazo izi ndithu. Mudzalira mpyooooooo!
Amasangwi ! Amasangwi! Amasangwi! Amasangwi!
Agonthankutu awa. UTM lero? Which bus is this? Koma MCP ili mu water. Ife ma blues sitikutekeseka. Omvotera APM tikumudziwa.
MCP has never been shaken in any election.
This tym like never before it’s gaining more votes from South n north in addition to their mighty central region .
MCP ikudza kusintha boma. all DPP mbava paulendo
Search your hearts. Search in your spirit if you are not creating a negative perception to take advantage of the illiterate masses by engaging their minds with trash.Ind you this happened between Brown Mpinganjira and a Chair
There is nothing new.The allegations must have facts
Mulira simunati,UTM and Chilima is unstoppable.