Email a copy of 'UTM UK wing elects office bearers, to hold fundraising dinner Nov 17' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'UTM UK wing elects office bearers, to hold fundraising dinner Nov 17' to a friend
Malawi Network of Religious Leaders Living With or Personally Affected with HIV and Aids (MANERELA) has expressed concern with the...
Kodi ku Malawi kulibe anthu oti akuthandizeni kuyendesa movementyo? Akunjawa anathawa dzikoli…..asiyeni tithana nazo tokha here……
Look like convicts in the red regalia of 1) UTM 2) EFF of Julius Malena and 3) People Power of Robert Ssentamu Bobi Wine the red uniform for the youthful millennials plus those in a quest for a ??? Future???
UTM ikugawana zida inu ndiye mukupanga fundraising ku Mangalande- za m’mbuyo mwa alendo. Kutengeka sikwabwino.
Masangwi said at the UTM rally in Mulanje and I agree “Mulomwe ndi Munthu Ochenjera…” Khomwe ankatokumana achina Mulli,Kaliati ,Masangwi Namapangana kuti APM ndi Osayamika Ayikepo Chilima munaliko?Ndiye pano muli Drain the Swamp …??Umadrainer swamp ukudyerera momo?
CHILIMA IS GOING NOWHERE.,…
muziona a DPP mu may muno mukapume mwatibera mokwanira
Mbava DPP pano akuganiza kuti tikuwaletsa kuba ndiye tikulakwa
Kkkkkkkk ! These guys are not aware that UTM is denfuct.
Is it really “den- funct’. Chilima wazunguza anthua spellings
Denfuct, what is it? Ma cadet!
Mukuona ngati mukati UK wing ndiye ife a DPP tichita mantha ndi chiledzelere wanuyo. Za ziiiii. Motowutu kuno unali wamapesi ndipo wazima.
Nsanje, Kodi kulibe DPP wing ku UK?????? Why can’t you just mind your business and support your party. Don’t you know that we live in a democracy. Mapesi or no mapsei, it is people’s choice and you should learn to respect that.
Ask Chilima to stop drinking too much because the party will charge its name to United TopiTopi Movement
Bola chiledzelele kusiyana ndi Maliseche !
Chilima mwamulephera basi . Nkhani ikhale ya kachaso basi? Saulosi ankamwa ndi Bingu that’s why Maliseche anamusankha. Musova
There names doesn’t sound Malawian to me
Koma sukulu ndiyofuniks chifukwa you need to know when to use do, don’t and doesn’t
Read your on post you see lots of typos
Hahaha, which name is Malawian, tell me is peter a Malawian name or is Lazarus ? Even yours
Trivia….politics of emptiness nonse…..focus on Malawi…things that really matter like how do we prevent currrnt scenarios where a President and Vice President agawana zida…how can we avoid this coz tax payers money is going to someone not working
Chichewa chake: kumeneko maina sakumveka achiMalawi kwa ine. KKK!
Mu Malawi mulibe aMakhalira, aMunthali, aMlanjira? Koma ma cadet wa!