Email a copy of 'Vendors clash with police in Malawi capital city: Fire tear gas' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Vendors clash with police in Malawi capital city: Fire tear gas' to a friend
Despite Big Bullets rejecting TNM’s offer to run an SMS promotion to enable the club raise funds for their CAF Champions...
Ok, achewa mwayamba kuyerekedwa? Mukuiwara kuti anthu akumwera omwewo ndi amene akuipanga Lilongwe kuti ioneke bwino.Ngati izi muipitiliza tisamutsa likulu kupitanso ku Zomba or Blantyre ndipo nzotheka.Kukumangirani parliament,Stadium,presidetial villa etc mukuona ngati mwafikapo? Mbole zanu mwamva.Mwaila kuti Kamuzu amakakamira kumwera chifukwa chokongola Bt + Kuchawe.Mudzakalira tsiku lina.
tsakulaninso ma besi ajatu kuti enawa akaphuzire maluso osiyanasiyana aja ndi kumapeza chochita . kodi nanga aliyense akakhala venda malo ake achoka kuti , bola kubesiko asakagwirenso mifuti ayi .but the idea was good.anthu koma adangokhala osakhululuka mumaona ngatikuti chilichonse amapanga KAMUZU chinali choipa komatu Ulendowu ndi wa tonse
Shaaaa ma venda akwa goliati bwererani mundichitsa manyazi pilizi. Ma venda a ku machinga kapitani kwa kapoloma. Kuno ndi kwa chakwera ndi abale ake a chewa ndi atumbuka
Just give them fines if found on street selling items thats all, they will stop all that rubbish!
No vendors cannot just occupy places anywhere they like. It’s illegal. But Lilongwe city officials do even worse things. The occupy plots all over for personal buildings or for eventual sale. Investigate the two friends – The Director of Finance (Mr Sibande) – A plot in Area 25, another in new Area 49, another in Area 43, two in Area 47 (one annexing old grave yard near Chigoneka Community Day Sec. school, another one along the same branching road, where he stays, just to mention but a few). The his friend the Chief Executive (Mr Hara) – Oh! plots everywhere… Read more »
Ambiriwa ndiwobwera kuchokera kumwera kosowa zochita. Kuba ndiye kwawo. Geni ya ma sweet usiku kuba.
mbava zachoka kwa goliati
kumadzavutitsana ndi apolice kuno ku lilongwe.fwetseki
Anthu akwagoliati wawo ndi ulimi ndi ma ofice basi, kuima misewu kumabela anthu amaona zotaisa nthawi. Mlesi nchewa kwake nkuvina gule basi akatopa ndi gule nkumabela wanthu ntwn, Nate ntumbuka xul ikamukanika kuthawa Ku kaya nkuzapisa wanthu mmatumba musova!
Azikuphulitsani Chomcho Mukuzolowela
Tinapumulako tear gas
pAja amapita ku chibvomezi or landslide ndi mfuti!
mavendof enawa si an hto ama bwanaku office..kale evdn ma line a mhc panalube zifha.ndala zogulitsa second cloghes or makala or mandazi etc zinali boo zinthu ndi a ngaazi hkb