Email a copy of 'Visually impaired Chanco graduate Fingani Mudzidze steals show at MCP manifesto launch' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Visually impaired Chanco graduate Fingani Mudzidze steals show at MCP manifesto launch' to a friend
Malawi government has faulted the Association of People with Albinism (APAM) over Saturday's clash between police and members of the...
Yona Yona Yona, siungathe kuthawa mulungu
umbuli
Chakwera yemweyo kuti wa wa wawaaaaaaaaa!
Go on …..proud of you..
Sikusinja, mwaiwala khang’ a John Zenasi Ungapake Tembo. The master manipulator, whose shadow follow LMC. Take care.
Ndaonavino kikkk Mfundoless We are in Democracy now,it was one party system so whatever happened it can’t happen now & the people who were doing that are no longer in MCP.NGATI AGOGO AKO AMATAMBA NDIYE KUTI IWENSO NDIMFITI? BWANJI OSASINTHA DZINA?
Are you serious? Is Cecilia Kadzamira not in MCP? How about Hildah Manjamkhosi? Has JZU renounced his MCP membership?
Are they in MCP Executive Committee or Management
Patrick Phiri
Are the people that you are mentioning still active in politics? Engage your brain before you write rubbish here.
Akuchokera ku mtundu womwe unadyerera ndi Congress, sanamve kuwawa ndiye kuti.
Awaso nawo zaziiiiii……….talakhulani momveka mukuti chani……..Nchoncho mungafusire MKAZi ndikukulorani inu…inu
where can we get the song please
WELL DONE FINGANI…PROUD OF YOU
Name is FUNGAI MUSIDZE
But this Fungai Musidze Boy was on tv a few weeks ago praising Chilima and UTM and dzana was praising Chakwera and MCP. How serious is he.
Unali usanabadwe kapena kuti nkhanza za chipani chimenechi sukuziziwa? mcp zimayi akakhala woyembekezera komanso mimba yake nkukhala yaikulu amadulitsidwa ma card a chipani atatu ati mimbayo ndiyayikulu kwambiri ndi mapatsa. A youth league inu sichoncho? Lero ndiye wina aziti chani? mukufuna kupweteketsa anthu ndi mcp
America is being run by the same parties that used to favour slavery. That segregated blacks, that banned women from voting. Times change, people change. Look around and find out who were the people responsible for such atrocities. One is Bakili Muluzi former secretary general. He is not in MCP anymore. Dr Ntaba. Lovemore Munlo. These were the people. A party does not kill people. It’s people in the party who do that. If u want to talk about what a party’s reputation. Look at MCP infrastructure. How was university of Malawi doing. How was govt run. How were thieves… Read more »
tikunena kuti those who were in MCP doing all sorts of bad things are the ones making noise in other parties. Chakwera was not there at all. Nanunso mwina mwabadwa kumenetu. This MCP is a tranformed party, come rain or sunshine ife we will vote Chakwera, 2019 bomaaaaaaaaaaaaa!!!!
Are you sure you will withstand the heat of MCP on Nyasatimes..??
The point is that those amene mumawapopa ndamene ankapanga nkhaza pano analowa kudzipani zanuzo he is not wrong look anthua anu mamachita kuwatama iwo sanenapo zimenezi mumakakamila zimenezo anthu oti simudziwanso kuti anchoka nazo nkhaza zawodzo kubwretsa kwanuko. So much that zipani dzanudzo mukamapanga nkhaza timadziwa kuti adanyamula katunsu wawo pano akumugwiritsa ntchito komwe adapitako kwanuko so he is right
Rember it not only you who experienced nkhazazo and who was alive that time but we all know
That was not the contitution of the party. It was rather the induviduals like those now in DPP who wanted to be recognised in the party. By then Chakwèa, Mia, Mkaka, Mkandawrre etc were not in management nor active at any level.