Email a copy of 'Wa Jeffrey says Ndirande is DPP stronghold, upbeat of by-elections victory' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Wa Jeffrey says Ndirande is DPP stronghold, upbeat of by-elections victory' to a friend
The Enlightened Christian Gathering Church (ECG) headquarters at the Pretoria Showgrounds in South Africa was a beehive of religious activities...
palibe zimenezo kuchipinda kwa chani ndiye ngati kuli kuchipinda osangolowa cha mutu bwanji abakha inu ku ndirande makata kukuyenera kusintha basi mseu wabwino kulibe iwe jefrey uziwauza anthutu za nzeru osamawangowanamiza azimayi anzakowo kuti miyendo mwamba tipange chitukuko
All what I can say is a Malawi ndife anthu ogona kwambiri. Dpp ikunenedwa apa mwa 50% anthu amuchipanichi ndi amene anali a mcp. Tandiuzani munthu mumozi wa mcp yemwe anali nawo mcp yakale ija. Anthu osnse who formed udf anali a mcp the very udf and old mcp people formed dpp. Uyo dausi apha anthu ambiri
Zoonadi mukulankhulazo Mamie,in fact, Blantyre yonse ndikuchipinda kwa mighty DPP.akutsutsa ndani?????????2019 m’bomansooooooooo.DPP woyeeeeeeeeee!!!!!!
Ndirande yes I can agree but the challenge at hand is lack of gifted speakers who can articulate government development agenda. People who can talk and impress people about Govt plan for the industrious youth of ndix. My fear is if we don’t spell out what we have done and what is in the plan , the ndix republic may start losing interest. Don’t give room to people who tortured the people of ndix. We have not forgotten
All the people that tortured you are in DPP, unless if you don’t know the history of Malawi. Dausi was body guard of Kamuzu, Ntaba was talking computer of old MCP and defended the regime left right centre, etc, etc. Tht’s why the killings of Chasowa, Njauju, July 20 demonstrators, etc, etc. If you support DPP you are supporting the old MCP. Nthawi ya atsamunda analiponso ena anatsilira mbuyo ngati inu ankasapota azungu woti ankaluza. So was the case in 1993 and 1994. Inunso mukuwoneka choncho kuti mutsalira m’mbuyo.
Hahahaha! Mwaswera?