Email a copy of 'Wake up call as Nomads held by Mangochi Select ' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

4 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
JOSEPH CHAGOMELANA
6 years ago

NDIZOSADABWITSA KUTI ANTHU MUKUNGOKAMBA ZA IFEYO MA BLUES, NGAKHALE ATOLA NKHANI AMATHAMANGILA KUMENE KWACHITIKA ZODABWITSA NDIYE ZA IFE MUKAMBAKAMBA MPAKA MUTOPA KOMA ENIAKEFE SITIKUTEKESEKA NDIYE PEPA NEBA USALILE VOMELEZA KUTI CHINGAMBWE CHAKUDWALITSA MUTU WACHING’ALANG’ALA KOMABE LIMBIKILA MWINA MAWA ZIDZAYENDA.

nomad
nomad
6 years ago

osadanda maule, phuma mulibe, inu pa easy….

pathfinder
pathfinder
6 years ago

kkkkkkkkkkkk thanks to a dubious penalty! just like the just ended league race. Mudzifunse nokha ndi ma game angati omwe anoma amapulumukira mma penalty nthawi yothaitha? ndiponso kafukufuku akuti ndi team ya noma yokha yomwe yawinira ma penalty ambiri koposa ma team ena onse. Warning! mu CAF sangopereka ma penalty osadziwika bwino, ndiponso palibe kukodzera pa golo, makamera omwe amatumidzidwa amakhala amphamvu. mudzayalika atakuchitani qualify chifukwa chokodzera pagolo. kkkkkkk mpaka mangoch select eti?

Zude
Zude
6 years ago

Mukakalimba Ku DRC mukabwela ndi 3-0,apo biiii,mukasenza zigoli moyipa.

Read previous post:
Simama top goal scorer wants to play in Super League

Top goal scorer in the Simama Premier Football League Division, Tonic Viyuyu has expressed interest to showcase his skills in...

Close