Kodi inu wandaleyi alibe abale ake oti atha kumulangiza zosatira za zimene akuchitazi kwa banja lake ndi abale ake. I have on some times listened to his arguments and position…. penapake zimakhala ngati penapake sipali bwino in the medulla oblongata….. akamuunikedi ameneyi ku chipatala.
Jamax
6 years ago
Take him to mental hospital please!! we are tired of his nonsense!!!!
james
6 years ago
shaaaa,koma Malawi,mmmmm kaya
Lincoln
6 years ago
Trust me, fodya wasuta nkuluyu is more than our nkhotakota breed
Yusuf
6 years ago
Peter and your Guard men, why arresting a foreigner without full investigations; Wandale is a MUST by nationality not a Malawian.
getrude
6 years ago
Lawyer Goba Chipeta, here is your client again. THAMANGANI NDI MA FILE
mvuu
6 years ago
Muonjezerepo mlandu wina olowa ndi kukhala Ku Malawi opanda visa
Kodi inu wandaleyi alibe abale ake oti atha kumulangiza zosatira za zimene akuchitazi kwa banja lake ndi abale ake. I have on some times listened to his arguments and position…. penapake zimakhala ngati penapake sipali bwino in the medulla oblongata….. akamuunikedi ameneyi ku chipatala.
Take him to mental hospital please!! we are tired of his nonsense!!!!
shaaaa,koma Malawi,mmmmm kaya
Trust me, fodya wasuta nkuluyu is more than our nkhotakota breed
Peter and your Guard men, why arresting a foreigner without full investigations; Wandale is a MUST by nationality not a Malawian.
Lawyer Goba Chipeta, here is your client again. THAMANGANI NDI MA FILE
Muonjezerepo mlandu wina olowa ndi kukhala Ku Malawi opanda visa
Even your…… ask him why ruling Malawi while he is not a Malawian.
He is a head of state kkkkkkk
Kodi a Wandale amasuta chamba???
Shaaa a president unali ndi passport yaku Malawi koma
Takidziwanichokani!!! Akulu Akulu kalelo adali ndi nzeru ponena mawu amenawa