Email a copy of 'Wandale rejects medication at Zomba mental hospital' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

8 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Toka
Toka
6 years ago

Mukuleka kuwagwira amisala akungozungulira mmatauniwa mukulimbana ndi Wandale munthu wabwinobwino chifukwa chani?

Chilombo
Chilombo
6 years ago

Mutulutseni Sanapenge uyu. Tikamuona akuthamanga mbulanda ndipamene titakuyitaneni. We know you don’t wanna arrest him but you’re trying to silence him so you put him in Rehab. Tryna take me to rehab i said nooo! nooo! nooo!

Kwali
Kwali
6 years ago

Please do not chew any food prepared from that hospital

Takwalakwa
Takwalakwa
6 years ago

Kukana Mankhwala ndiye misalayo!!!!!!

MBWFC
MBWFC
6 years ago

komainu wandale wakulakwirani chani kkkkkkkkkkkkk, musiyeni aphwe madzi

Munthu Wankulu
Munthu Wankulu
6 years ago

Where is our Ministry of Health on this? What does WHO say? Can you please guide us on the individuals rights and obligations in accessing health services including mental health. What are the basics? Who brings a patient to hospital? I think Wandale has 100% right to seek a second medical opinion. I rest my case!

DPP BOMA
DPP BOMA
6 years ago

Kkkkkkkkkk kkkkkkkkkk

Awize
Awize
6 years ago
Reply to  DPP BOMA

Kukana mankhwala ndi chizindikiro cha matenda a misala. Chimodzi-modzinso kukana kuyezetsa magazi ndi chizindikiro chachikulu kuti munthu ali ndi HIV/ AIDS m’thupi mwake. Mphunzitsi wanga anandiuza kuti ukhala mlenje pamene ukasaka, nyama iriyonse yomwe imathawa ndi yodyebwa ndi ndiwo ndithu koma yomwe ikaona munthu simathawa imeneyo si ndiwo (its dangerous) usayiyandikira pafupi ikuvulaza. Wandale has a point, but he must prove beyond reasonable doubt that he can indeed be harmed by Govt medical personnel at Zomba Mental Hospital. Otherwise, more rarely, a patient is at liberty to choose whether to receive medical treatment or not. Zikavuta mankhwala timakakamiza kuti munthu… Read more »

Read previous post:
Mwawi, Mvula miss Malawi Queens first match in England

Australia-based netball icon Mwawi Kumwenda and Joyce Mvula – all shooters – who were left behind in Lilongwe to sort visa issues...

Close