Email a copy of 'Wandale set date for setting his  Thyolo, Mulanje ‘government’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

21 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Haila
Haila
6 years ago

Tilipambuyo pako tonse kuno kutyolo ndi mulanje tachokamo muboma la Malawi

memory
memory
6 years ago

Why is the Malawi government treating this man with kid gloves?

santana
santana
6 years ago

And a whole journalist in the name of Muheya who claims to have attended school of journalism can waste his precious time writing about this nonsense.

Jamax
Jamax
6 years ago

kkkkkkk!!! my dear Wandale you are even failing to come up with the proper name of your country it’s like a sentence, ok in the first place where will be your capital city, your National Radio Station, your Paliament Building, your Airport????????? kkkkk!!!! kapena muzibwerekera!!!!!!!! Inu a Wandale Reserve Bank yanu zidzangokhala Nkhokwe za ku Luchenza etiiii kkkk nanga State House yanu idzangokhala pa Sapitwa etiii??? Surely, this is the right time to laugh a bit WANDALE Woyeeeeeeee!!!!!!!!

#iamyournextpresident
6 years ago

Kodi mwati chani aNyasatimes, who is this Wandale?new country in Malawi,zikuchitikadi, so Mulanje and Thyolo will be an independent state, is that what you are saying????

youna
youna
6 years ago

Weed is talking

NO NO NOSENSE
NO NO NOSENSE
6 years ago
Reply to  youna

KKKKKKKK FOR SHIZO

Kaloswe
6 years ago

Nanga PITALA akalamulila kuti? Ife akumalawi sitingalole munthu waku Thyolo Country kuzatilamulila

Akuzike
Akuzike
6 years ago

Let the truth be told this guy Wandale wapenga misala. Those who have studied mental issues will agree that munthu wamisala amafika poganiza kuti ali ndi dziko lakelake!

MUPOSITOLI
MUPOSITOLI
6 years ago

This is pure madness. Chamba chikuzunguza anthu pa Malawi. This stupid man just want to gain fame for nothing. This noise will never take us far. Mark my words.

alpha
alpha
6 years ago

Pali mavuto ambiri ku Malawi nthawi ino amene akufunika anthu okonda dziko lao athandizepo. Zomvetsa chisoni ukamamva anthu ngati Wandale akubwera ndi nkhani zopanda pake. It is a waste of our time kumatiwerengetsa nkhani zongotayitsa nthawi ngati izi mmalo moti tikanapanga zina za phindu pa moyo wathu komanso moyo wa ena m’dziko lathu la Malawi. Democracy ndi yabwino chifukwa imalemekeza ufulu wa munthu koma anthu ngati Wandale ndi openga. odwala komanso osathandiza pa chitukuko cha dziko. Boma la anthu oposera 14 million si masewa so why allowing chopenga ngati ichi kubweretsa chisokonezo? Do you know repossessing land mu njira ngati… Read more »

Lt. Fraser Chakhaza
6 years ago
Reply to  alpha

Why are people so concerned and against Vincent Wandale and the people of Thyolo and Mulanje to declare the two districts independent and sovereign states? Is this the first time we have heard this?The people of South Sudan were part of Sudan but decided to have an independent state because they were being sidelined by the north due to the color of their skin (black) and most of them are not Moslem. Western Sahara block away from Morocco in similar circumstances. Taiwan was part of mainland China but chose to break away and form its own independent state although China… Read more »

alpha
alpha
6 years ago

Inunso a Chakhaza mukuoneka kuti nkhani yoti boma ndi chani muli nazo kutali kapena kuti simuzindikira konse.
Mosakunyozani bwana, tayetsani mwayamba kuwerenga mabuku ena ndi ena kapena mutafunsako anzanu kuti akuthandizeni kumvetsa what a sovereign state is.
Pepanitu bwana koma ma comment anu akundipangitsani kuganiza kuti ndinunso mbuli ndi wodya fodya ngati wandale tikunenayu.

harry
6 years ago

Well written Chakhaza, I second you.

Read previous post:
Nkhotakota stops Hamra from oil mapping exercise in Lake Malawi

Nkhotakota District Executive Committee (DEC) has  asked United States of America (USA) based Hamra Oil Holdings to put its oil...

Close