Email a copy of 'Wanderers appeal Sulom’s ruling: Challenges 'selective justice'' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

12 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Real supporter
Real supporter
6 years ago

Wanderers is right to appeal this is indeed a miscarriage of justice. For a start Mzuni didn’t enter the venue, neither did they lodge a formal complaint to law enforncers. Besides they could’ve played the game under protest just like their counterpart did.

Ndayizivei
Ndayizivei
6 years ago

A Butao sakulakwitsa popanga appeal. Mzuni ndi mu ground momwe osalowa basi wa ku lodge kwawo kenaka ku hospital after akuwuzidwa ndi wina wa Sulom. Izitu zikupha mpira pa Malawi pano. Chilungamo chinayenera kuwoneka basi

Symon Mkweza
Symon Mkweza
6 years ago

Williams Banda ndi chitsiru cha bullets, tiona ngati ana ako osuta fudya wa Nyasawo atenge league

Nostradamas
Nostradamas
6 years ago

Josephy chagomelana ndiwe Mbuzi ya munthu ulipa pressure ndiwe ndi team yako chaka chonsechi chikho or cha plastic ulibe neba ukunyadila ziti?

Nostradamas
Nostradamas
6 years ago

Nyerere kumavomera zithu mukalakwitsa kodi mipalayo mukuoneka Ngati ndinu anzeru kuposa aliyese? Aaaaaaaa chitani manyazi a Butao kumavomela zinthu zikalakwika mukupeleka chitsanzo chotani Kwa ena amene sanalowe super league? Manyazi akugwireni a Butao kkkkkkkkkk

JOSEPH CHAGOMELANA
6 years ago

KAYA REPLAY OR NOT, KAYA NEBA AFUNE OR ASAFUNE, KAYA SULOM IFUNE OR ISAFUNE KOMA NOMA NDI KAWAWA MOTI CHIKHO TATENGA BASI NDIPO AMENE ZIKUMUNYASA NDI AMENE AKUMVA KUWAWA KOMA IFE TILIBE PROBLEM.

Delilah Samson
Delilah Samson
6 years ago

Bvuto ndi SULOM. Williams Banda is a supporter of Bullets and it’s all clear. This man Williams Banda is very unethical and biased towards BB – I can tell you if this involved BB and Mzuni- the judgement could have been different. Williams Banda need to go, he is very incompetent and a supporter of BB – Given all the facts provided, Wanderers deserve the 3 points and Mzuni punished for not following procedures. You cannot make judgements based on heresay- there was a SULOM rep in BLK what did he say concerning the match – why in the judgement… Read more »

Mzozodo
Mzozodo
6 years ago

Mzuni, the team that was asaulted say the judgement is fair? Koma pa Malawi

pathfinder
pathfinder
6 years ago

kkkkkkkkkkkkk Muyezo umene umawayeza nawo anzako nawenso amakuyezera ndi omwewo. Wanderers imachita organize masopota omwe anasiya kusapota bullets kalekale kuti azikachita ziwawa game ina ili yonse ya bullets pa chilomoni ground, ndicholinga chooti bullets ikhale ndi mbiri yachabe komanso azilandidwa ma points ndikutulusidwa mu fisd cup. Kungoti ife a bullets sitimatha kulozana zala olo tikudziwa akutiyipitsira mbiri ndi ndani. Lero takujudulani ndi yomweyonso ndipo iwalani, mapointsi a ulele simupatsidwa.

san
san
6 years ago

Wanderers want to tell us that they want to set a precedent that a team can be intimidated and go ahead play -loose the game and nothing done by authorities. Mukunamatu inu!! just pay mitre yo, re-play the game and stop intimidation.

Read previous post:
Red Cross Malawi constructs toilet worth K5.5 million to keep girls in school

Lack of proper sanitation facilities and absence of exchange rooms in primary schools are some of the obstacles that hinder...

Close