Email a copy of 'Wanderers club now in orange colours: Nigerian on trials' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Wanderers club now in orange colours: Nigerian on trials' to a friend
Tendai Tambala is the new Miss Malawi College of Accountancy (MCA) after being crown during the pageant last weekend, beating...
Koma neba! Zoona mpaka Boko Harram?
Apa nde mukuti mudziwina poti mwapeza left winger? Kodi mukufuna kutchuka chani tikuonerani mmalo motukula ma player anu omela dzinangwawo mukukatenga Boko Harram akudyereni tindalamato basi, bola takuuzani.
guys ngati tikukanika kulipira ma prayer anthu uyu ndiye tinkwanisa manoma malizani tonse ta be fowardto kkkkkkk
neba waganiza zoti bokoharam ikuthandiza ku Malawi kuno mpira afuna azaone kuti ndalama za b4 ward wasunga ndani kuti azakameme anzake a bokoharam ameneyu usamale ndiye bolanso surestream
Honestly speaking NOMA Ganizani bwino, our football has not yet reached commercial Level, we are still developing in football, and you are ropping in a player to occupy a place that you would otherwise develop a Malawian Player……..retrogressive thinking indeed.
Neba umva kuwawa chaka chino!
Bola asakhale wa Boko Haram
Zakunja sidilu koma kukanika
That’s football development others should emulate
your Welcome Tulalope from Nigeria .. We profoundly like your perfomance and tactics .