Email a copy of 'Wanderers continue title charge, beat Moyale: Malawi TNM Super League' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

4 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
pathfinder
pathfinder
6 years ago

Don’t get too excited yet manoma. Ife maule tagwetsa Silver pa number two, mwatsala ndi inu tikulandeni udindo wathuwo. Nkhondo iyambika saturday likubwerali tikakukutumulani. Tidzasiyana ndi 4 points koma inu mdzatipilira ndi game imodzi. Tikadzasewera gemuyo yomwe tidzawinenso, mudzatisiya ndi one point. Samalani manoma, maule akubwera. mukangoyerekeza kuchita draw olo kuluza mnyengo imeneyoyo, ife mapale league tatenga.

Mighty Be Forward Wanderers Fc
Mighty Be Forward Wanderers Fc
6 years ago

Zomwe timayembekezela zikuchitika,Tithokoze Ambuye.apiltilizeso kutidalitsa.

matela
matela
6 years ago

Tikumva tseketseke ife -keep the pot boiling the lali lubani boys. please get ready for bb the coming weekend

goodwellbanda
goodwellbanda
6 years ago

Kawawa noma

Read previous post:
Red Lions ends Silver unbeaten run: Malawi TNM Super League

League strugglers Red Lions produced a five star performance to register one of their most amazing victories after beating Silver Strikers 1-0...

Close