Email a copy of 'Wanderers hit back at Cameroonian player: ‘Asu is not special’' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

50 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Kingster Bella
Kingster Bella
8 years ago

KODI MUCHITE KUMUSANKHIRA KOKHALA. KOMA A MALAWI UMPHAWI. MUPATSENI NDALAMA ZAKE MOGWIRIZANA NDI ‘CONTRACT’ MGWIRIZANO WANU.
ZONVETSA CHISONI, MUMAFUNA ZINTHU ZABWINO PAMENE NDALAMA MULIBE..

‘LODGE’ YA KU MALAWI NKUMATI NDI YA PAMWAMBA..

MUPATSENI NDALAMA ZAKE. ZIKAMUTHERA NDI YEKHA KOMANSO NDI ZAKE..

A MALAWI ZONVETSA CHISONI KWAMBIRI. KULEPHERA KUMUPATSA $7000 INTERNATIONAL PLAYER..

Madalitso
Madalitso
8 years ago

Nawe Thindwa usazigulitse pamtendo wabonya,what is beforeward?sangamatulutse ndizopunsa zomwe adabwerela business not kudzangogawa ndalama mumulipire pa ntchito wagwira masiku ambuyo anthu oyipa inu eti!

mchenga patrick
mchenga patrick
8 years ago

Timaziwa kuti neba wapenga nayo 70mita. Nanga ku Tigers kunja poti munati malire ndi June mulimba? Ife kwathu ndikuona

Francis Banda
Francis Banda
8 years ago

Musova

ninja tek
ninja tek
8 years ago

ha….ha…hhahaa.i was expecting it
.mpaka ma burundi.mungawapatsenji mukukanika welfare ya abale athu a konkuno.ka 70 mitre kangokula pa kamwa sikanali ka ndalama kopenga nako misala mpaka kumagula ma player kunja mavuto ali thooooo.usova wakula watha neighbor.

zizwa
8 years ago

Aziplta Thindwa wabwera kale

muhamad sulumba
muhamad sulumba
8 years ago

mphwanga, unya uwona.

jimmy zakazaka
jimmy zakazaka
8 years ago

musampatse ndalama ameneyu azipita kwawo. mukuona ngati timamuonela kukondwa? ngakhale tikuphonya pagolo goal keeper palibe, nkwathu kuno, a kanaji amatilowetsabe nkani akwiya nawe. paja enafe tinazitembelera po dumper BB kupita kwa neba kusatila kananji. pepa mzanga Asu mpa malawi pano. such is life.

Nyakwawa
8 years ago

Let him pack and go.
We have enough armoury in Muhammad “Defoe” Sulumba

zomwezo
zomwezo
8 years ago

Koma Neba,yhaaaa ulimbe ndi munthu ameneyu.Ndinkangokuwonatu nthawi imeneyija ukudumphadumpha. sopano.wamkaka uvuta kumwedwa kwake apa.ukati ugwire kapu Atsu ali pa mbalipa kufunsa zake,ukati usewere ndi neba Atsu uyo wafika akufuna zake. Koma neba unakamutenga kuti uyu.ife sitingamuthe kwathu kuno.mpaseni zake azipita ztiyipisila mbiri uyu.

Read previous post:
Time for politicking, over- College members of DPP

Executive committee members for the ruling Democratic Progressive Party’s (DPP) youth wings from Bunda and Natural Resources Colleges say time...

Close