Email a copy of 'Wanderers inch closer to Malawi title with 3-1 win against Mzuni FC' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Wanderers inch closer to Malawi title with 3-1 win against Mzuni FC' to a friend
Kukoma Diamonds have increased their chances of get closer to the southern region Rainbow Paints League championship after beating their...
Congratulations neba. league mwatenga baasi palibenso kunenera mwina. Ndasiya kudzilimbitsa mtima. Bullets lest start making serious preparations for next season. Lets face it, master security and red lions siilimba pamanoma. well done nomads, you deserve it. you fought so hard with an intent to win the league and you have just done that. kaamwani wamkaka.
bola tikanatenga ya pa table ija kusiyana ndikuumbudzidwa chonchi kkkkkkkk, Manoma ulendo wa ku paradizo
KODI ASULOM MULI NDI MAU? TAKUTHIBULANI PAMODZI NDI KACHINGAMBWE FC WANUYO, MANYAZI BWAAAA? IFE NDI NYELELE MAFANA MAFANA MUKUCHEPA!!!!
ana amwano aphedwa kudererera akulu shaa chigoli choyamba cha sulom chachiwiri cha bullets chachtatu cha noma
Neba akuti bwanji? wakhala ukuti ukubwera pambuyo, nde mpakana lero?
Neba Neba atipeza azinka natilondola pa National Bus Ife tili pheeeeeeeee mu ndege kkkkkkkkkkk
kkkkkk neba wamva nyunyunyu, neba vamva wawisa , neba wamva fwefwefwe, neba mutu sukugwira