Email a copy of 'Wanderers maintain their lead, BB and Silver secure wins: Malawi TNM Super League' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

6 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
chitima
chitima
6 years ago

neba … pamwambapo osakomedwa ! tikweleko ife..

nyerere
6 years ago

Neba sungatipeze silver akubwela pamaso pako ukumuona koma

Wa Maule weniweni
Wa Maule weniweni
6 years ago

Pali anthu enafe Mulungu amasiya dala kutidalitsa chifukwa amadziwa kuti ndife opanda phindu. Kungotsogola chabe koma chiphokoso chino!!! Nanga ikanakhala BB yoti anawina ligi for a record thirteen (13) times tikanamwa madzi? A reminder please, five games to go. By the way if BFW happens to win the league that would be after a record eleven (11) years (typical of Asernal).

Mzozodo
Mzozodo
6 years ago

Nzeru za u chawa za ma supporter a Bullets

Mighty Be Forward Wanderers FC
Mighty Be Forward Wanderers FC
6 years ago

koma neba mose munayambirakuti wankuru akubwera m`pakana lelo osangosiyakunena bwanji??,manyazi mulibe

Kalirani
Kalirani
6 years ago

Neba Chenjera wamkulu akubwera pambuyopo

Read previous post:
Silver in 3-0 emphatic over Chitipa United: Malawi TNM Super League

A double substitution in the second half steered third placed, Silver Strikers to a 3-0 emphatic win over bottom of...

Close