Email a copy of 'Wanderers, Silver sail through to next round of Malawi Carlsberg Cup' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Wanderers, Silver sail through to next round of Malawi Carlsberg Cup' to a friend
In an attempt of clarifying issues that the country’s electoral body claims were “grossly misrepresented” in a local newspaper article...
usova neighbour Nyerere ndi Nyerere!!!!!!!!!! Chaka chake ndi chino uganyula bule chaka chino neighbour kkkkkkkkkkkk
Zimpweteke ndani,osawina ya dzana ija bwa????????ngati muli madoloo,,,,,,
Zikatha mbewa anona ndi swiswiri tiwayamikirebe,
Mofaya noma!!!
Ma NOMA be forward ever, you must win all games remaining in the first round and turn the tables. MA NOMA WOYEEEEEE!
Nyerere ndi nyerere basi Ana achepa awa
Max Bullets imatero kulalata kuti ife ma noma tisamete msanga, kani mumafuna madzamete ndinu. Mtima umemewu musausiye. Noma woyeeee.
Mbewu yogwera kupindura
NYERERE NDI ANA AWA KUCHITA KUSANGALALA CHONCHI, NYINYANI AKULU ANZANU HEDE
wakwiya ndi mfiti!!!!!!!!!!!