Email a copy of 'Wanderers to recruit assistant coach: Technical panel reoganisation' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

13 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
innocent
8 years ago

Technical is too much. Jimmy zakazaka apite ku technical. kungotola zinthu zothaitha ngati zimenezo. amenya pati ?

kennedy jailos
kennedy jailos
8 years ago

zozunguza coach apa ayi. kananji has started well with his troops!!

Abraham Lincoln
8 years ago

waistage of tym

mwanapeter
8 years ago

Mano azanga tigwirane manja kuthandiza team ndi ndalama mwamva. Za supporter ma peto chonde tidzivota ulendo uno noma ikhale wani. Tilipo ambiri koma ulesi tichepese tikonde team. Komanso Yasin Osman achoke munthu osokonedza kwambiri ameneyu. Adzisokonedza kananji Y kukakamira ufuna udzipedzako ya fodya eti. If wanderers imaonongeka ndi ka osmanka. Musachulunsenso technical panel cholinga mudzitibera dola. Lanjesi abwere coz madefender anthu ali boh koma afupika tipedzeko wa mtali, Rafik mussa, adzimenya ndi suman pakati, sulumba ndi asu kusongolo, kaliati ndi kaziputa mbali, lufeyo, sanudi, kaipa ndi malumbo kumbuyo. Mlimbika akumalimbikira national team yokhayokha ndiye adzikhala paja ameneyu. Chipuwa pa goal.… Read more »

Lost
Lost
8 years ago

Bravo!

Charles Elias
8 years ago

Nthawi yanu manoma ndalama zakuchulukilani, kenako tizangova kuti mwagula jet yoti muzayende nayo chaka cha mawa mu CAF.

Mzozodo
Mzozodo
8 years ago

Phodogoma you might be right but how much can Malawi teams pay these guys compared to what they earn there?

Phodogoma
Phodogoma
8 years ago

Please think of these Malawian guys from south africa like John Maduka, Ernest Mtawali and Patrick General Mabedi. These guys are good and they can bring a difference in our soccer circle . We are tired of the recycled coaches who are doing nothing by the end of the day..

Chakuchaku
Chakuchaku
8 years ago

Musaonongesotu,tayamba Bwino.

misheck jasi
8 years ago

Akananji athu akufuna kumangokuyuzani chenjerani

Read previous post:
Women private parts fetching K14m, Mchinji murder tells court

Medson Selemani who murdered his cousin Janet Chitedze and mutilated her private parts at Shadreck Village in Mchinji district says...

Close