Email a copy of 'Wanderers to take part in Chief Minister’s Cup in India' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Wanderers to take part in Chief Minister’s Cup in India' to a friend
Central Zone Basketball League (Cezobal) has reached out to multimillionaire Malawian prophet based in South Africa, Shepherd Bushiri to help...
Timu koma iyi, moti pano matimu M’Malawi muno ndi awiri basi : Number one Noma(Nyerere) mwana wake ndi Wizard. Amenewa ndamene amasewera mpira weniweni osati basketball ya Maule kumene chikagwere ndi komweko, ayi. A Ndudu/ Fodya BB taphunzirankoni mamenyedwe osati ngati gofu.
Jaffali Chande will join the team to India, outside Africa.Manoma woyee!!!!!!!!!
that’s my team
That’s why i love you guys. I ‘ll never leave wanderers alone.
Nyerere tikukufunirani za bwino zonse. Uwu ndi mwai wanu ngati timu komanso ngati ma players. Kasonyezeni kuti ku Malawi anyamata aliko odziwa mpira. Kuchitabwino siwekha but a contribution of several the keeper, defenders, mid-fielder strikers ngakhalenso masapota, a coach ndi wena. Mukapeza mwayi agawireni anzanu osati nokhanokha. Tisachedwe kuloza zala anthu wena. Maso athu patsogolo. Tiyeni tiwone zoofoka zathu ndi ndi zotilimbikitsa. Pasakhale kukhomerelana apa. All the best -supporter wa Nyasa Bullets
The Wise People’s Choice…osangoti People’s ayi that is too General, But The “Wise”
More fire nyelele, tikakoke chikho chakuIDIA!!
GO KONKO GUYZ!!!!!!!!!!!!!!!!!
Noma ndi more fire nsanje siumuna maule tifunireni zabwino inunsu Ku cap mumatibweretsera zoipa. Chaka cha mulungu chaloza komaso ubwino wake tikabwerako bwino opanda ngongole.
Abulets Ndi Anthu Oipa Kwambili Ngati Satana