E-Mail 'We will not be silenced by Mutharika outburst - Mayaya' To A Friend

Email a copy of 'We will not be silenced by Mutharika outburst - Mayaya' to a friend

* Required Field


Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...
Please share this Article if you like Email This Post Email This Post
  Subscribe  
newest oldest most voted
Notify of
MaKopa
Guest
MaKopa

What can we do for the government for what the government can do is corruption

Mathasimo Muhiye
Guest
Mathasimo Muhiye

Mr. Mayaya you are justing wasting your time and resources. As someone has already said, kodi inu mwapanga organize mademo angati? Munapindulanji with your demos? Inu tikukudziwani mumatumidwa ndi MCP. Musiiyeni APM alamulire dziko li.

KARU UNITED
Guest
KARU UNITED

Tiye nayeni!

Che Ngana
Guest

For Ur Imformation Mayaya.Peter Sakuyankhula Kuti Iwe Uwope Ayi.Go On Do What You Know Best Koma U Will Never Succed.Wapanga Ma Demo Angati Pamalawi Pano.Yomwe Inapindula Ndi Iti.Uchitsiru Wake Mmayamba Mwatukwana Kaye Kenako Ulendo Kunseu Angakhale Ndinthawi Yokupangani Attend Zopusa Zanuzo Ndani??Tiyeni Timange Malawi Osati Kupasula.

Che Ngana
Guest

Team Mayaya Sopano.Peter Akakhala Chete Bwanji Wakhala Chete?Akayankhula Bwanji Wayankhula?Amalawi Akamamutukwana Peter Mayaya Kumakhala Kulibe.Akamva Zoti Amalawi Akutukwana President Mmalo Mowalondolera Amalawi Ziti Achite Kuti Nadandaulo Awo Amveke Mayaya Amati Amalawi Akulira. A Mayaya Pa Moyo Wanu Ndi Anthu Angati Omwe Amakutukutukwanani Kukunyozani Inu Mkumawalemekezabe???Amalawi Kodi Mmene Timawatukwanira Ma President Athu Muja Timafunanso Ulemu?Wayankha Mmene Ifenso Timayankhulira Palibepo Nkhani Apa.Mmafuna Azikupilirani Mpakana Liti?Mpatseni Ulemu Pa Nthawi Yake.Ngati Sakuchita Bwino 2019 Muzavotera President Yemwe Azasinthe Zinthu Kwa Masiku Awiri Mukufunawo.

Mlomwe
Guest
Mlomwe

KODI KALIATI DZINA LAKE LIKUPEZEKA KU UNIVERSITY OF MALAWI?NANGA KONDWANI NANKHUMWA?AWA NDI AMODZI MWA ANTHU OSAPHUNZIRA KOMA AZIYAMIKA MLOMWE MZAWO.PITALA NGATI ULI NDIMAKOBILI ADAKUITANA NDI NDANI KU MALAWI?NKHOPE YA UFITI NGATI IMENEYO

little jojo
Guest
little jojo

Billy Mayaya is the most attention seeking I know. He is positioning himself for 2019. He will stand as an MCP candidate, just like Jessie Kabwila did. She fooled us that she was an activist for academic freedom, yet she stood for MCP in 2014. Bily will do the same. When APM was quiet, Billy and company accused him of being arrogantly silent. Now APM has spoken, Billy and company are accusing of being arrogantly noisy. Billy Mayaya is educated, he should tell us which country in the world has ever developed through demos? America? Britain? China? Billy, tell us… Read more »

Benson T Phiri
Guest
Benson T Phiri

Days are numbered -Chilichonse cholo ndi pothera pake

little jojo
Guest
little jojo

Billy Mayaya is working for his political future in 2019. He will stand as an MCP mp. This was what Jessie Kabwila was foing, masquerading as an activist to gain political ground. When APM was not commenting on anything Billy Mayaya and company accused him of being arrogantly quite. When he has spoken Billy Mayaya says APM is arrogantly shouting at Malawian’s. Mayaya is one of the greatest attention seekers I have ever known. His strategy is yo maje as much moise as possible to be noticed by MCO and hence position himself well go 2019. Any one who will… Read more »

chadza kwayani
Guest

Akamanga apa ndiye mwafotokoza monveka bwino. Tiyeni amalawi tikhale anthu ochenjela. Tisamangosekelela zina zilizonse zomwe munthu wakamba pomaopa kuti ndi presdent. Tiyeni timuuze ameneyu kuti dziko ndichinthu chantengo wapatali .

Kapena akuyesa kuti ndi nkalasi eti? Hey zitengeni bwino chifukwa mwagwirizila udindo waukulu . mukumangoti jepetujepetu mmalo mopanga chitukuko bwanji

Ndatha wanu CHADZA KWAYANI