Wanderers Will be rescued by refereeus as usual.Determination is what Will in this years Super League,money will not win any team a game this year.Mark my words,the worst to come for Beforeward Mighty Wanderers.
yazula
8 years ago
Iwe Ashraph Kammwamba nkhani ili apa ndi ya noma, zakozozo ku noma konko, otherwise udzaona polekera
Adam christon Masamba
8 years ago
Udzikhala ndi mkhalidwe polankhula, peter mponda angakhale mbuli? Mpira umaudziwa iweyo? Ndisazakumvenso? Udzikhala ndi moyo odzichepetsa.
A mponda siyani kuyankhula yambani kuchita. Mukuonetsa umbuli kuyankhula zambiri inu muganiza mungapambane ndi noma? A wise speaks coz there is something to say while a fool speaks coz he wants to speak lyk wat mponda does.
opportunist
8 years ago
Akudalira chani mkulu ameneyu
mwanangu
8 years ago
BB WILL BE CHAMPS AGAIN
Ellaton Chimtengo
8 years ago
mukupha nyerere zmenz guyz, wawo ndi wapakamwa koma pa ground zimawavuta. red zakazaka. woza mponda, woza chimaimba zako ziwiri mzolembalemba
Makanja congress party(MCP)
8 years ago
musaope muona polekera. A mponda anthu anakuuzani kuti akulu ndi mdambo inu mumvekere sabola wakale sawawa.Go ahead & be beaten again.
BIG MAN
8 years ago
Mukaphanya zimenezi, umodzi umodzi wanu uja ukapangitsa Mlimbika kutenga Red Card!!!!!, I remember mau ako Mponda onena kuti kwa BB tikungofuna draw, but lero kwa Tahit akuti sukuiopa!!!! Go ahead Mponda!!!!
Wanderers Will be rescued by refereeus as usual.Determination is what Will in this years Super League,money will not win any team a game this year.Mark my words,the worst to come for Beforeward Mighty Wanderers.
Iwe Ashraph Kammwamba nkhani ili apa ndi ya noma, zakozozo ku noma konko, otherwise udzaona polekera
Udzikhala ndi mkhalidwe polankhula, peter mponda angakhale mbuli? Mpira umaudziwa iweyo? Ndisazakumvenso? Udzikhala ndi moyo odzichepetsa.
nyerere zimakokera ku una,sure samala,midzodzo ikakhala ikununkhitsa stadiun.mwinanso chiswe chifika kudzachitira umboni.