Chaka chino tiona zodzizwa ndii matimu omwe amati ndi ang’onong’ono. aBFW alira nawo kale ndipo BFw kwao kalirira ma REF kuti amawada , Game iyi Ref game iyi Ref Mmafuna maRef adzikukonderani Mmene imachitila Fam ndi Sulom,? A Sulom takondwera poti BB mwayipanikiza ndi matimu okhaokha akuluakulu. popeza yikuoneka yofooke yiferetu yimeneyo, siipuma chaka chino. sabata yamawa Blue Eagles pena Mzuni matimu apamwamba ap o Biii wizard, Onse chenjerani tiona mbonaona za ku England. Inu pheee tione a song by matafale and Let us wait and see ( Steve Banda) liwewe mwana Iiwewe.
wizards yomweyo..mponda’s philosophy now is working
Gd luck wizards
Chaka chino tiona zodzizwa ndii matimu omwe amati ndi ang’onong’ono. aBFW alira nawo kale ndipo BFw kwao kalirira ma REF kuti amawada , Game iyi Ref game iyi Ref Mmafuna maRef adzikukonderani Mmene imachitila Fam ndi Sulom,? A Sulom takondwera poti BB mwayipanikiza ndi matimu okhaokha akuluakulu. popeza yikuoneka yofooke yiferetu yimeneyo, siipuma chaka chino. sabata yamawa Blue Eagles pena Mzuni matimu apamwamba ap o Biii wizard, Onse chenjerani tiona mbonaona za ku England. Inu pheee tione a song by matafale and Let us wait and see ( Steve Banda) liwewe mwana Iiwewe.
Nzuni wizards
I’m behind them
Nyasa BB woyee woyyeeee the # 1 team
mmmmm koma chaka chino ziriko ndithu