Email a copy of 'Women private parts fetching K14m, Mchinji murder tells court' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

30 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Pee
Pee
8 years ago

Poor cursed boy……………..wshing u a happy stay in there……….Mulungu akonze moyo wako mwapaderadera

KULEMERA APEREKA NDI MULUNGU
KULEMERA APEREKA NDI MULUNGU
8 years ago

Panopa Satana akukuseka waima patali apo. Iwe ndende ndiye waipeza kale. Mlandu wotere aliyene akhoza kugamula, kusiyana kukhoza kukhala pa kaperekedwe ka chilango.

Kondwani
Kondwani
8 years ago

koma achitsiru awa, inuyo mutakhala nayo 14mitayo anthu sangakudabweni?mukalembe jc muli kundendeko.

lucia
lucia
8 years ago

Mmmmm kaamba kofuna ndrama now you find trounbles that’s good my be its not this girl you did alots off

Keen Observer
8 years ago

Shame, my fellow country men there is no way the so called “witch doctor” can give you K14 million, where in hell can a sangoma get such money?????? Kulemeratu sikukhetsa mwazi nanga now look umenewu ndiye ulemelero eti?

nyasa boy
nyasa boy
8 years ago

Kusauka kwadziko ndiamthuomwe chisoni padziko lonse lapansi

Paul
Paul
8 years ago

A DEVIL at work using people. Demonic power led him to do this evil.Lord have Mercy.

MELINDA
MELINDA
8 years ago

poor little boy.kulemera ndi sukulu komanso ku mtundu.ngati ambuyako anafa nawo umphawi,iwe nde ulemera?utichimwitsa kapolo wa ndalama iwe.

taona ndi maso omwe akufotokoza kuti iwe ndiwe mwana wa JEZEBEL,YUDAS CHIDZUKULU CHA KAISALA.KKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKKK

Manase
8 years ago

Poor boy. Kulemera kothamangira ona anzako achina Kasambala, Lutepo, Ndovi, Namata, Mphwiyo alibe ufulu muntima. Apwitikizi ali ndi mwambi amati “quem quer tudo perde tudo” amene amafuna zonse amaluza zonse

Jimmy juga
Jimmy juga
8 years ago

Malo molemela walowa mmavuto adzaoneni . Wayamba kuoneka ngati wamisala zakutembenukila.wazidula moyo phwanga.

Read previous post:
Malawi player chasing Golden Boot Award in Europe

Malawi’s top women football star in Europe Tabitha Chawinga is set for another milestone this season in Swedish top league. Chawinga...

Close