Email a copy of 'Zakazaka rejoins Nyasa BB and signs a 7 months contract' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Zakazaka rejoins Nyasa BB and signs a 7 months contract' to a friend
Youthful and promising Malawian up-coming dancehall music artist 'Ababa Surgeant' real name Harris Mthipela has started working on his mission...
Pezani zina zochita amwene.. u will not go anywhere ndi mpira waku MALAWI.. START BUSNESS
a jimmy mwabwerera ku kampopi fc apa ndi ulendo waku midima basi thabwa ndilosayamba ku chingambwe fc ko mapanga awiri avumbwitsa mungovomereza kuti munapima basi
Olo akanamusayinitsa contract ya miyezi iwiri. Mwana ameneyu wamwano kwabaasi, anayitaya bullets ikumufuna kwambiri kumayesa ngati ku noma kuliko bwino, mapeto ake ankangodya bench. Panyero pako mwanawe, bwelera kumanoma kwakoko.
I wish you all the best of luck. Who knows one day you may do well.(Strong Supporter of Noma)