Email a copy of 'Zomba taxi operators unhappy with Unima over car hire services' to a friend

* Required Field






Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.



Separate multiple entries with a comma. Maximum 5 entries.


E-Mail Image Verification

Loading ... Loading ...

Sharing is caring!

15 Comments
newest
oldest most voted
Inline Feedbacks
View all comments
Cyclops
Cyclops
8 years ago

GG ndi deal, ma donors amafunanso cheap labour, ma car hire ena kudula kkkk

georgejuma
8 years ago

Akutsekula zimakalata zamayera zopikisana mu holo akuluakulu a IPC adatisimikizira kuti ntchito imeneyi ndiyochuluka sangapase car hire imodzi ; apereka kwama car hire atatu. Moti ntola khani wa bungwe la ICAP analipo patsikuli. Nde tikudabwa mukaperekedwe ka ntchitoyi. Na Malawi sazakhonzedwa !!!!!!

gan
gan
8 years ago

nsanje basi a malawi y cnt u go with ur pajero zolowesa fumbi mkatizo ku GG akazithamangitse muwone

mbwangalambwangala
mbwangalambwangala
8 years ago

I am also coming with my korora in very good condition but wihout shocks and one door to a left side does not close ndipha makwacha sopano kweee

george
george
8 years ago

Amalawi munthu wa GGali open kwa aliyene inu ngati muli 4×4 pitani ku office kwawo ku lilongwe kaya ku Blantyre akakupangani sub hire ife kuno taziona ku lilongwe pa mbowe filling station akuyesedwa magalimoto pitani mufufuze mwa biwi muipeza GG ikuthandizani siyani jerous amalawi palibe car hire ingakhale ndi 4×4 70 funasani pa biwi pafupi ndi ENTYRE ndipamene pakumadzadza magalimoto ndipo akumayesera pa mbowe madzulo aliwonse

Bololo
Bololo
8 years ago

Tax guys. lol. Pali ndalama kuchuluka zochitika

Stalla
Stalla
8 years ago

Malawians!!!! I have never seen a 4×4 vehicle at the zomba taxi rank, zichokera kuti? you want the university to hire those not so roadworthy cars for a survey? come on this mentality has to stop if we are to progress, kumangolira zilizonse basi. This behavior is common in the public service you hear of a cleaner or a clerk or a secretary complaining kuti sakupita ku field because aPS or adirector akungoyenda okha zoona? What will you do ku fiedlko when you are not even qualified for the job.

buyache
buyache
8 years ago

And I don’t see any problem by awarding GG with the contract cause this taxi guys are not organized…

harrinyah
harrinyah
8 years ago

hahahahah,there’s abig reason why zomba car hire owners were sidelined…2much kupondana nokhanokha when u hv subhired avehicle from ur frends company…mwaganayo basi..pitani ku statistics akakutengeni…idiots..GG waiphura basi..no nsanje

Chalaka Bakha nkhuku singatole
Chalaka Bakha nkhuku singatole
8 years ago

Do you really need to have physical cars to win a tender? As long as the GG Car Hire provided enough evidence that it can provide such vehicles then I don’t see any problem. What if this firm has links with other car hire companies that have these best vehicles? A Malawi nsanje!!!!

Read previous post:
Sisqo and Dru Hill to perform n Malawi

Multi-platinum selling American music group, Dru Hill, together with lead singer Sisqó, will perform in Malawi’s capital Lilongwe on December 12....

Close