Email a copy of 'ZZZzzzzzz… Bored MPs fall asleep listening to Malawi President Mutharika' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'ZZZzzzzzz… Bored MPs fall asleep listening to Malawi President Mutharika' to a friend
Malawi Police in the commercial capital Blantyre have managed to arrest suspected criminals who have been terrorizing ginnery corner including...
Koma nde inabowadi. KKKKKKKK
MOSE IMWE MUKUNENA PETER NDIMWE VINDERE! IMWE UKUMUTONDELANICHI UPULEZIDENTI
ain’t surprised at ll.those who does not like the current president shall use anything to show their dislike of him. Assertions that MPs went sleeping indicate that the speech was empty is a shameful lie. this is a plat form over which critics can possibly use to settle their goals. among all the reasons as to why one could sleep during such a time, how certain can we be that lack of substance in the president’s speech is the one which sent these MPs sleeping? malawians, lets wake up from our slumber and embrace some civilization.if we are not for… Read more »
kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk
Kukomera kwake akutsogolera kugona ndi leader of the house George Chaponda.
Boring speech
Yet you want long speeches, Asankhwi
The last speech of the financial 2015/16 year lasted only 17 minutes whilst this year was just too much…just imagine it lasted almost 1hr 30minutes !
ZINTHU ZO SIZINAKHALEDI BWINO.KOMA ZIMENE MUKULANKHULAZO MUZIPITITSA LILIME LANU KU CENSORSHIP BOARD MUSANALANKHULE.
MALAWAI NEEDS PEOPLE LIKE BOBO.
Kwa inu mukunyozanu.Kodi akadakhala ngati Bambo wanu mukadawanena zoti anali kuchbwenzi?…Kodi inuyo simunagonepo kwina kwake?..Nde kuti munali ku chibwenzi?
Kod Chaponda akadakhala kuti ndi relative wanu,nkumva anthu akumunena kuti anagona kuchibwenzi inu mukanasekelela?Bambo anu mwinanso amagona ku church,olo malo ena ake chifukwa mwina chakutopa,kodi amakhala kuti anali kuchibwenzi?..mayi anu olo akazi anu olo amuna anu mwina nawonso amasinza,nkugona ku church or ku msonkhano,ndekuti anali kuchibwnzi?