Email a copy of '100 Ethiopians arrested in Karonga: Five Malawi citizens nabbed for aiding illegal entry' to a friend
Loading ...
Email a copy of '100 Ethiopians arrested in Karonga: Five Malawi citizens nabbed for aiding illegal entry' to a friend
Carlsberg Malawi Limited has increased prices of its alcoholic and non-alcoholic beverages by 14 percent and 23 percent respectively with...
ayi malo ndi ambili, enafe tinachoka kumeneko kudzakhala ma iligo kuno ku ingalande. Ndiye malo anga mumupatse mzibambo mmodzi ineyo sindidzabwelanso! komanso amalawi ena ndi ma iligo ku joweniko remember!
ayi malo ndi ambili, enafe tinachoka kumeneko kudzakhala ma iligo kuno ku ingalande. Ndiye malo anga mumupatse mzibambo mmodzi ineyo sindidzabwelanso! komanso amalawi ena ndi iligo ku joweniko remember!
I agree, Malawi is too small to have them in our country too!! eeyah, abwelele kwawo!!
ai imeneyi siyogwira fans imeneyi apane isadzayambilenso kungolowa basi akuona ngati malawi ndiyofiyira eti apolisi muwapane alire chiethiopia anthu amenewa.
Malawi is too small please let these people go back homes
Osawasiya akafika kuno ku joni amanyada amatilipira ma 300rand pa wk agalu amenewa,amatitenga amalawi ngat zitsiru.mission yao inali njira kt azibwera kuno ku south africa
sadamvetse amenewa amaona ngati game yalero ili kuno kumalawi.amabwera kudza chemelera mpira
Kodi madili zonyozana zachani amalawi akufunako madola munthu nmozi $_$50 kunfikisa Ku zareka nde ukanyamula 10 sibasi waoloka inu muziti atumbuka madilu anzanu akulemela osawanena a cashgat wa bwa akuyanbisa zonyozamitundu anabadwila muuhure alive bambo ati amupase mwambo
Kodi a MALAWI mumafuna kusangalatsa ndani? mudzasowa kothawira tu ndi nkhondo mukuphika ku mudziko, ndi sonkhana sankhana…. kuzunza ma Africans anzanu choncho? chonsecho akudzutsani pa AIR Malawi ndi ma ETHIOPIANS omwewo!. kodi mumati mukutani mukamatero? mumadziona ngati muli ku EUROPE? pa LAMPEDUSA kapena??? mxii! asiyeni anthu adzidutsa. and it is high time, a MALAWI tidziwe kuti mzako akapsya ndevu mzimire mawa azazima zako. mudzasowa kolowera inu sure ! mwina mudzakwera ndege kumapita kutsidya kwa Nyanja>…////////////////////////! kaya! change change ONE AFRICA for Africanss! kodi ndinu chiluma panokha?? za u goodgirl simunasiyebe?
Pali.za utumbukanso apa? Anthu ena anabadwa ndi uchitsiru basi eti? Shame on yo u man!!!!!!!