Email a copy of 'Balaka again! Malawi Police arrest teacher for sexual assault on pupil' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Balaka again! Malawi Police arrest teacher for sexual assault on pupil' to a friend
Malawi government decision to head count each and every civil servant has met with resistance from some quarters amid fears...
koma guys penapake lets use our common sense zoona munthu 44 yrs kukakomedwa ndi kamwana ka 11 yrs,thats bullshit vuto lake mijombo mukapalitsa palitsa mipaliro yanuyo mumaona ngati mwafikapo basi.but guys lets respect our sociaty
everything ku balaka wats wrong with u there behave urself pls
zimamukomela thats y amangopitapitabe kwa teacher ko….fodya et
Mwana wa standard 3 zoona, ma guy ma hule onsewa? In Malawi, you can screw as much any size, colour, shape etc.
Mwanayo anatopanazo?Bwanji sanaone tsiku loyamba kuti ndi zoophya koma wadikidira mpaka kumukulisa nanyongo ndikumaulula bwino?Kungoti apa chilipo chomwe anthuwa anayambana basi.
what on earth”””|||::@@@@@@@ koMA ANTHU ENAWA AMAGANIZA BWANJI MPAKANA PAMENEPO…. NO NEED OF GOING TO COURT FOR DISCUSSIONS JUST ARREST HIM….. NO PROCEDURES…..
WAMANGIKE AMENEYO
Midyomba sizodabwitsa ndi khalidwe lanu anthu akumwera. Zigolololo too much. Mtsikanayunso zimamukomera osaulura first day bwanji? Because of jando u teach your children to have sex with elderly people from a tender age. This 11 year old knew what she was doing. Anavinidwa kale ma offals am’bamboyo samamudabwitsa mwanayu akuzidziwa kale otherwise akanaulula first day. Southerners are a disgrace to Malawi. 11 years in standard 3 zoona? These days?
Izizi anyamata amasiku ano ziziwachitikira kuumira maningi ndawa.Nanga inu munthu paka zaka 44 osakwatira amatani? Ifeyo pamenepo ndiye kuti tili ndi ana atatu kapena awiri.Anyamata inu akazi sapha munthu zikwatirani panthawi yake mofulumirako kupewa zoterezi komanso ana amakula bwino bambo ukadali mnyamata wamphamvu.Uyuyu just look suppose he marries today mmene mwana aziti 10yrs old basi bambo akuchita retirement approx 55 to 57yrs.Anyamata moyo wanuwu simukuganizira bwino komanso wabanja lanu.Ana amafunika akumvetsetse kholo kukoma kwazaka zingapo.Komanso mkazi amvapo chani ukwati 10yrs munthu ukalamba wayambika?Wake up anyamata mukutichititsa manyazi kwajinji.
Balaka Balaka………why? she is your daughter sir.
Komanso m’Balaka alimotu mahule otchipa, bwanji osatengako mmodzi?
Plz timatumiza ana ku Sukulu kukaphunzira osati kukakwatiwa
Athu Otelewo Azilandilitu Sentence Osachedwa Nao Mucastody Ayi Life In Prison Basi, Ameneyo Silast Born Wake.Male Teachers Muzikhala Ndi Umuthu