Email a copy of 'Balaka man arrested at his engagement ceremony' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Balaka man arrested at his engagement ceremony' to a friend
Sometime in January 2013—eight months after then president Joyce Banda, Finance Minister at the time Ken Lipenga and Reserve Bank...
ndiye zopusatu osamudikira amalize kaye bwanji chinkhoswe cho mtima wachikang’a umenewo
u foolz,mzanu asadye katundu
agalu inu!
Iwowo sakuona kut ntchitoyawo adailephela.ngat adamulephela kumupeza before ukwati adakamusiya amalizitse basi.coz ili limakhala special moment yamunthu.
Its not fair mukadamudikira adye kaye then zinazo pambuyo
Muthu ndioipadi paka kulepheresa chikondi cha zake za sanje basi
Apolice achinyengo inu mukusiya kumanga mbava
Zomwe zkuwonnga chuma chaboma athu okumba ma bilion akusiyidwa koma okumba mkhuku. Ten years in prison ziko lapansi likomela opata nonse amene mukugwila mtchito muma unduna aboma ndinu bava zoipa koopsa ndatopananu
Itsgood koma mukanadikira kayezinazi mwina ndi nsanjetu
Zina ukaona kambanga mwala. Ntchito ikhale imeneyo koma a Police musakhale kuti mukudyelera maso mkazi wa mnyamatayo.
i agree with 41,42 and 43.