Email a copy of 'Bishop Msusa elected president of Episcopal Conference of Malawi' to a friend
Loading ...
Email a copy of 'Bishop Msusa elected president of Episcopal Conference of Malawi' to a friend
Prayer is communing with God and if it is without sincere desire or soul or Spirit in it then it...
RIP ZUZA & BEST WISHES TO MSUSA. tonse ndife olengedwa ndi Yehova. aliyense ali ndi zofooka ndi zolimbika zake but blessed are the pure in heart for they shall see G O D
Anthu a mulungu solimbana nayo mubvulala ndithu
Anthu aku Mangochi amadana ndikuwatola moti apa mukungotukwana poti ndi mchigulugulu.You will only understand them only when you follow the Bible and get your foreskin removed.Apo bii simudzatimvetsa.
Mlolo, you must be a King or Queen of the devils. Be warned something very very Bad will follow you if you do not repent. How can you call Man of God ‘Mfiti’? Do you have any evidence?
People of mangochi being fair? What a stupid and misplaced comment
Ndizoona Chisoso ndavanso kuti kumwera kukhala snow yoopsa ija ng’ombe zimakwilirika nkumafa.
Missing a point buddy, is being critical wrong? what is wrong is pointing out about degree of someone’s stupidity? Mediocrity is letting Malawi down. Let us speak when we can.
Congrats His lordship. My the soul of the late RIP
Choka iwe nawe ndiwe chindere chakufikapo wa kozgana na munyako yula
mr/madam mmihavani, ndinu munthu womvetsa chisoni. u think bcoz anadzudzula ulamuliro ndiye kuti anakuipirani? inu ndiye magulu omwe mukanafuna mabishopu akanaphedwa mu 19920 podzudzula MCP. Shame to u. mudzafa udyo mukamalimbana ndi atumiki a Mulungu.
Kudzudzula sikolakwa koma kulakwa ndi kutukwana